Ufulu Civil servants loans.🇲🇼
*Ufulu finance limited*
Pezani ngongole ya chiongoradzanja chochepa ku Ufuni finance limited.
Ngongole ya Ufulu.
1. Mumalandila ndalama zonse zomwe mwangongolazo. Siimadula processing fee
2. Mumalandira ndalama pasanathe maora 72.
3. Ngati mukufuna kupanga top up loan yanu, zimatheka.
4. Mukapeza ndalama zimathekanso kupanga settle loan yanu.
5. Mumaloredwa kutenga ngongole ina ngati muli ndi affordability koma kuthekera kupanga top up palibe
6. Chiongoradzanja chathu ndi 4.5% pamwezi. Mwachitsanzo kutenga 1,000,000 pa miyezi 12 mumadulidwa 123,374.46 pamwezi ndipo pa chaka mumalipira 480,493.52 ngati interest.
7. Mutha kutenga kuyambira 30,000 mpaka 5,000,000 bola mukhale ndi affordability yokwanira.
8. Tili ndi ma office ku Blantyre, Lilongwe,Mzuzu, Zomba, Kasungu ndi Karonga.
Ngongole za Ufulu Ndizama Civil servants okha basi.
Kuti mupeze yanu lero Tiyimbireni kapena kutumiza uthenga ku Whatsapp pa 0982875460.