MCHINJI HOT MUSIC FOREVER MIX MACHEZA
WELCOME TOMCHINJI HOT MUSIC FOREVER MIX MACHEZA
Ino ndi group ya music mixed macheza Komanso kugawana zinthu zatsopano zosiyana-siyana🔥🎹🎧
Malamulo a muno ali motere👇👇🧑⚖️🧑⚖️🧑⚖️
(1)👉 kunyozana muno ayi ❌ ukapezeka remove
(2)👉 kuponya zolaula kapena zotukwana muno ayi ❌ ukapezeka remove
(3)👉 kuponya ma Link a ma group ena muno ayi ❌ ukapezeka remove
(4)👉 muno timalola ku typer ndi ma Record omwe/vn
(5)Osaponya zinthu zoopsa muno monga: zithunzi ndi ma video olangiza anthu akuphana kapena ngozi chifukwa ena amadana nazo wina angatifele pano ena ndi a matenda a bp.koma ingobweletsani nkhani yachitikayo wina akafuna zimenezo,mutumizileni ku inbox
(6)muno zilankhulo ndi ziwiri chichewa ndi chizungu
(7) aliyense ndi mtola nkhani payekha osadikira admin okha kuponya nkhani, nyimbo,ma video,ma comedy,ndi Zina zotero,apa tibwerezenso 👉🏿koma osati zolaula chonde.
(8)👉ngati walakwitsa mwangozi,pepesa mwachangu.
(9)osaponya za using'anga muno❌
(10) nkhani za ku inbox zisakhudze group
(11) Ukambilana nkhani za ndale pano ayi zimabweletsa mikangano❌ si grop la ndale lino
(12)pa sanday/pa sabata)ndi pic day,aliyense akupenphedwa kumaponya picture yake kuti tizidziwana
✍️✍️.
🤝 Tiyeni tikhale ngati banja limodzi choncho aliyense asunge malamulo ophwanya malamulo remove. ulemu wanu abale monse 🧑⚖️🤜🤛🙏🏻🙏🏻🙏🏻🤝🤝🤝