Zee❤️Tz fashion collection 💕😍
Hello, dzina langa ndine Zione Kangawa ndimakhala Ku Lilongwe . Ndimapita ndekha Ku Tanzania kukatenga katundu amene mwandituma. Zimatenga masiku awiri kuti katundu afike.
*Malamulo*
1) Yekhayo wasankha ndikupereka deposit adzapezeka pa list .
2) Ndimatenga katundu yekhayo mwandituma size , design komaso mtundu wa katundu yemwe mwasanga .
3) Mukadzasokoneza size , design & colour ya katundu yemwe munagula dziwani kuti sivuto langa ndipo palibe chomwe ndidzachite pa vuto limenero .
4) Katundu wanu adzatumizidwa kutengera ndikomwe mwasankha kuti nditumize {CTS , Speed , Post office & Bus } . Kwa omwe muli around Lilongwe mudzatengera mtown ndikafika .
5) Katundu ndimaoda yekhayo Kwa amene apereka deposit .
*Dziwani*
-Kuti deposit ndi theka la ndalama wakatundu yemwe mwa oda .
-Osayitanitsa katundu ndalama yonse palibe yowombolera katunduyo.
6) Ndidziwitseni msanga ngati Pali kusintha pa katundu yemwe mwasanga ndisana gule .
7) Njila zoperekera ndalama ndi izi ;
- Airtel Money Agent Code
126143
- Airtel money number
0999317878
- TNM Mpamba
0884205833
- National Bank account
1006973694
Zonsezi zilemba *Zione Kangawa* . Mukamatumiza Ku number muike yodulila
8) Katundu adzatumizidwa pokhapokha munthu akamaliza balance .
9) Mukalipila tumizani screenshot ngati umboni .
10) Kulephera kumaliza balance katundu wanu akafika mpaka next oda , katundu wanu azagulitsidwa ndipo deposit yanu simudza bwezeretsedwa .
*Zikomo posankha Zee Tz fashion collection ndimakunyadilani kamba Ka support yanu* .