חפשו באינדקס קבוצות הוואטסאפ של WhatsAd כדי למצוא את הטובות ביותר.
בערך 1 תוצאות (0.42 שניות)
Takulandilani alendo anthu ku group lamacheza Atsikana ndi Anyamata Malamulo ali motele angati walowa kumene akuyenela kutumiza picture ndi kudzfotokozelaso muli 2 muno link ya group lina sitimalola kupatula lanthuli 3 osasankhana osankhana machezedwe muno nkazi kapena mamuna ali ndi ufulu kucheza amene akufuna muno 4 muno ma video olaula sakuloĺdwa ukatumiza remove 5 osamulowela munthu inbox yake asadavomele kuti mupite ukapezeka ndi remove 6 Sunday ndi pic day aliyese amaponya pic osatumizayo tsiku limenelo amatulutsidwa 7 muno kungonkhala osamayankhula kapena osakometa remove 8 nkhani ya topic aliyese atha kulemba topic koma osalemba topic wina ataponya kale chonde 🗑️🗑️🗑️🗑️ 9 chonde ngati mwawona kuti wina sadakuchezeleni bwino pezani admin akuthandizeni 10 muno nkhani zaku inbox zisafike pano pa group zithele konko 11 osatumiza ma sticker please ma sticker ena amankhala wonyoza nde osaponya please 12 mayina awa muno osatchula munthu ngati hule, fiti,kapolo ndi ena 13 osanyoza chipembedzo chazako muno ukapezeka remove Zikomo kwambili achibale nose muno ngati likumveka group chifukwa cha inuyo tiyeni tidzicheza Kutsatira Malamulo kut masiku ako opedzeka pano achuluke🥰😘❣️💕💞💖