חפשו באינדקס קבוצות הוואטסאפ של WhatsAd כדי למצוא את הטובות ביותר.
בערך 1 תוצאות (0.42 שניות)
Ndinu olandilidwa ku apabass music reach up the talent one Nthawi yanu yobooleza ija yakwana. Kwa amzathu amene muli ndi luso lamayimbidwe ndipo mukufuna luso lanu lipite patali yankho lake lapezeka. Apabass music yakhoza njira zomwe zingathandizile ma artist omwe akufuna kubooleza. Iwowa ayambisa Top Ten challenge imene inu oyimba muziwatumizira nyimbo zanu ndipo iwo aza azizapanga post nyimbo zanuzo mma platform awo; Facebook page, WhatsApp channel and their WhatsApp group. Akapanga post nyimbozo azizasankha potengera ndi ma likes a nyimbo yanuyo. Umu ndi momwe azisankhira nyimbo from number 1 up to 10. Nyimbo yanu ikapanga qualify mu top 10 list imeneyi a Apabass adzaipanga promote pokaisiya ku 1 Mzati FM 2 Angaliba FM 3 Gaka FM 4 Ufulu FM Ndipo nyimbo yanu ngati yachita bwino pa competition imeneyo malandilaso ndalama ngati izi Number 1 adzalandira ndi 20k komanso internet bundle & promo kwa week yonse Number 2 adzalandira10k komanso interview & promo kwa week yonse Number 3 adzalandira 5k komanso interview & promo kwa week yonse Registration fee ndi K5,000 yokha. Mutha kulumikizana nawo powalembera message pa WhatsApp: [contact hidden] Nyimbozi atolera from lero kufikira pa 5 March 2026 ndipo competition idzayamba pa 6 March 2026. Chamba chinachilichonse cha nyimbo ndichololedwa. NOTE Sadzalandira nyimbo yomwe mwaimba pa beat yopanga download osachotsa ma tag Join their WhatsApp group using the link below 👇 [link hidden — subscribe to view]?mode=gi_t Mutha kupanga follow kuti ma update azikupezani moyambilila 👇 [link hidden — subscribe to view] Follow their Facebook page https://www.facebook.com/share/1DKQYY1aUa/