MAVIK GROUP 2
❇️ welcome to MAVIK COLLECTION
❇️We sell goods from china, south, Zambia n Tanzania
*za china zimatenga mwezi kuti zifike,,,,za south 2 wks...Zambia week and Tanzania week*
❇️Goods here are on retail only .... available n taking orders
❇️Katundu yemwe palibe ndimatenga kwaokhawo omwe andituma komaso alipira
❇️Ngati tikuoda you pay half inayo zikafika ngati Pali Zina zomwe mukufuna ndionetseni inbox ndikusakireni
*Ndalama sitibwenza ngati zavuta mumasankha china*
❇️Lipirani ku *1067425* ( kelvin tembo)
*NB account 1002627597*
Zikomo 🙏🏼