KUGAWANA NYIMBO MWAKATHITHI 🔥🔥
*WELCOME TO KUGAWANA NYIMBO MWAKATHITHI*. 🫂🎧🎧🎼🎵🎵🎶
*MALAMULO ATHU ALIMOTELE👇🏼👇🏼*.
*1.🛑ukangojoina kumene group yambakaye waponya pic... Yako ndikuzilongotsola dzina lako ndikomwe ukuchokera*.
*2.🛑Tilemekedzane wina ndinzache posatengera mtundu kapena chipembedzo or kochokera*.❌❌⛔📛🚫
*3.🛑No ma videos kapena zithunzi zolawula muno even ma voice notes❌❌⛔📛🚫ukangopedzeka remove🎬🚮*.
*4.🛑No any foreigner groups/links, ma short videos or stickers muno ayi❌❌⛔📛🚫ukangotumidza basi uwona nsana wanjira🎬🚮*.
*5.🛑ndiudindo wawina aliyense otumidza nyimbo muno osamangodikira ma admin okha kuti atumidze nyimbo❌❌⛔📛🚫*.
*6. 🛑Then usanapemphe nyimbo yamba kaye waponya nyimbo zomwe iwe ulinazo ndipo ife tizakuthandidza the same time*.
*7.🛑Kupempha mowirikidza koma iwe osatumidza zimenezo ayinso❌❌⛔📛🚫ma camera akakuwona 👀basi remove ndiyomweyo🎬🚮*.
*8.🛑Ndipo osatenga nawo gawo pa maprograms amenewa timasazikana naye mosayang'ana nkhope🤣❌❌⛔📛🎬🚮*.
*⚠️🚸WARNING: ngati wapedza kt group lakiyidwa🔐🔐🔒🔒osafunsa kt why?❌❌⛔📛 Udzalandira remove 🎬🚮ndekuti ma admin akukonza zina zake zosemphana ndi group*.
*#. ✅✅Tsatilani zimenezi kt matsiku anu okhala muno achuluke musanawone nsana wanjira ngati omwe adawona John chilembwe kumandala😉*.
*#. ✅✅Machedza wez koma nyimbo kathithi...*.
*WROTE BY ALL ADMINISTRATOR OFFICCERS, MWAKOMA NONSE🥳🥳💃🏻💃🏻🤼♀️🤸🏻♀️🤸🏻🏋🏻♀️🙊🙌🏻🙌🏻*.
500+ membersActive this monthYAO