Ищите в каталоге групп WhatsApp от WhatsAd, чтобы найти лучшие.
1 результат в каталоге групп WhatsAd
TIPEZE KU INIBOX TIKUPASENIYAKUTIMAKWANU MUVU
Проверенная ссылка-приглашение, данные об участниках и опции рекламы на WhatsAd.
MULI OLANDILIDWA NDIPO KHALANI OMASUKA KOMA IFE MA ADMINI TIMAKHALA NDIMA CONDITIONS AMENE MUKUYENELA KUWASATA MONGA NGATI MA MEMBERS A GROUP LINO 1 osapanga send link ina iliyonse pa group kupatula la group lino 2 tikakhala ndizochita pano pa group ngati pic day komaso ndi zina zambili ngati simukutenga nawo gawo asala yake ndi remove 3 osapanga send zithuz zolawula kapena video 📹 yolawula 4 ma recording saloledwa pano 5 voice chat kapena kuti call sizoloredwa 6 osapanga send sticker iliyonse 7 member aliyese akuyenera kukhala ndima message opitilira 10 patsiku 8 anthu omwe simukufuna kukhala pano khomo ndilotsekula mukhoza kutuluka 9 zako ngati akuyambisa mapokoso kapena akukutukwana musabweze chifukwa mukatelo mukhala limodzi pa ulendo 10 khalani anthu okondana ngati ndife amalawi tokhatokha 11 matumizidwe amafilm ngati film yatumizidwa osayibwelezaso 12 ngati muli ndi number yomwe ikufunika kupanga add tumizani ndipo ipangidwa add GROUPULI LIMALAMULIDWA NDI ANTHU AWA OYAMBA DESMOND WACHIWIRI MR PEACE WACHITATU SHONGA WACHINAYI ASIFA WACHI NUMBER 5 LAMIN YAMAL. NGATI PALI VUTO APEZENI ATHU AMENEWO AKUTHANDIZANI NDINE WANUWANU DESMOND DMINI 🙏🙏🙏
TAKULANDILANI KHALANI OMASUKA CHONDE TSATANI IZI KUTI. MUKHALITSE PAMALO PANO👇👇👇 1. Link ya group Lina ayi🚫 2. Zolaula kuno ayi🚫 3. Zoyambana kutukwana ayi kunyozana ayi🚫 5. Ma voice recorder ayi 🚫 6. Ndiudindo waliyese kuponya filim TIPEZEN ADMIN KUTI TIKUTHANDIZENI ZAMAFILIM OMWE MUKUFUNA👇👇 099130220 Mukafunaso VIP ILIPO MTENGO K2000 AKU JON OR MAYUNITS🙏🏽