Ищите в каталоге групп WhatsApp от WhatsAd, чтобы найти лучшие.
1 результат в каталоге групп WhatsAd
😂😂♨️
Проверенная ссылка-приглашение, данные об участниках и опции рекламы на WhatsAd.
*NYIMBO ZOTAMANDA KOMANSO KUKWEZA YEHOVA*
Malamulo a Muno ------------------------------ (1)Kupempha ndikutumiza nyimbo. (2)Nyimbo zake ziyambire 2010 kumatsika kumusi. (3)Osatukwanana wina ndimzake timalimbikitsa ubale muno. (4) Osatumiza link or ma Photo olaura kapenanso zosemphana ndi group lino muzachotsedwa. (5)Osanyozerana mtundu kapena chipembedzo tonse ndi amodzi. Komaso osaponya ma sticker muno ayi (6)Ndi udindo wa aliyense kutumiza ndikupempha nyimbo zakale koma ngati mwafuna zatsopano pemphani ku inbox ena azakupatsani komweko. (7) Ma voice note siololedwa muno koma zikavutitsitsa kuti mufuna nyimbo nde mutu wake simukuudziwa funsani admin aliyense kuti mumumvetseletse Voice note ndipo akusakireni . (8)Osatukwana muno tili ndi anthu akulu akulu azaka zapakanthawi omwe amafunika kuwalemekeza. Tiyeni titsate malamuro kuti tipitilize kusangalara ndinyimbo komanso zochitika zotikumbutsa kale lathu .
🌳🌳🌳🌳 Takulandilani kuno ku group la ✍️✍️ KUCHIMAKE KWA MA LINKS 💪 💪 👫👫👩❤️💋👩🌴🌴🌴🌴🌴 🎄🎄🎄🎄🎄🎄🎄🎄🎄🎄 🫧🫧 Malamulo anthu ali motere💦💦💧👉👉👉 🍀🍀🍀🍀🍀🍀🍀🍀🍀 1🌳🌳✍️ Ngati mwalowa kumene mu group lino mukupemphedwa kuponya 📸 Pic 📸yanu 🙋🏽♂️ dzina lanu🙋🏽♂️komaso komwe mumakhala🏜️kuti tikudziweni✍️✍️ 2🌳🌳✍️ndi udindo wa aliyese kuponya ma link ✍️✍️ 3🌳🌳✍️Ano simalo opangila business kapena ndale ❌❌ 4🌳🌳macheza ndi oloredwa❌❌ 4🌳🌳✍️Osaponya ma video ngakhaleso ma pic olaula❌❌ 5🌳🌳✍️Ma sticker siololedwa❌❌ 6🌳🌳✍️Ma VN ayi❌❌ 7🌳🌳✍️ Zilankhulo zololedwa muno ndi English komanso Chichewa 8🌳🌳✍️ Ngati mwayambana kwinako zisafike muno ❌❌ 9🌳🌳✍️ Ngati mwakondana Tengelanani ku imbox 😂😂 10🌳🌳✍️Osalowa ku imbox kwa munthu popanda chilolezo✍️ 11🌳🌳✍️ Sunday iriyonse timakhala ndi 📸 PIC DAY📸kuyambila nthawi ya 08:00hrs⌚mpakana kufikila nthawi ya 21:00hrs⌚✍️ 🪼🪼🪼🪼🪼🪼🪼🪼🪼🪼🪼🪼🪼🪼🪼🪼🪼🪼🪼🪼 🦚🦚Mwakoma nonse nkhalani omasuka😃😃😃😃😃💃💃💃💃💃💃💃💃💃💃💃💃💃💃💃💃💃💃
[contact hidden]