Ищите в каталоге групп WhatsApp от WhatsAd, чтобы найти лучшие.
1 результат в каталоге групп WhatsAd
Group Ino ndima posta nsapato zimene zili readily available Ku Blantyre kuno Katundu timatumiza kwina kulikonse across Malawi on your desired courier (CTs, VIP, SPEED, AXA etc) at client's cost. Ngati mukufuna timupatsile munthu make sure munthuyo ndi mmodzi and is a trusted person wanu. Parcel imodzi sitilola kuti akutengeleni/ kupatsa anthu awili. Kugula tikuyambila 5 pairs and Above. Omwe mwazikonda feel free mundiyankhule nthawi yabwino. Sindimasunga katundu without Payment We reserve the right to not do business with anyone under ground of disrespect, foul language and immoral cyber behaviour. Once payment is done, send proof of payment to my inbox (admin). Do not make payments before you confirm availability of the sizes and design of slip-on you want. Those using courier, once admin shares a receipt with you, make sure you don't lose it or pass it around this compromises the safety of your parcel. MUNO SITIMABA, AMENE MWALOWELA ZIFUKWA ZINA OTHER THAN KUPANGA NAFE BUSINESS MUDZITULUTSIDWA
Проверенная ссылка-приглашение, данные об участниках и опции рекламы на WhatsAd.
Takulandilan khalan omasuka mumo sitiba ai osaopa okaikila osalipila kuopa phokoso No refund just exchang☺️
Takulandilan khalan omasuka kulikonse matumiza okaikila osalipila madana n phokoso No refund just exchange