Ищите в каталоге групп WhatsApp от WhatsAd, чтобы найти лучшие.
1 результат в каталоге групп WhatsAd
Pano ndi pa group la dza mpila only malamulo agulu aliyense amadziwa cholinga chathu ndikuika ma sewelo ampila pa tsogolo ALiyese ali ndi ufulu oyangula pano
Проверенная ссылка-приглашение, данные об участниках и опции рекламы на WhatsAd.
Qr8aaw5e41a
Cholinga Cha group ndikukambirana nkhani zokhuza dela lathu lamakanjiri kundale zadela ,chitukuko komanso mavuto amdela MALAMULO A GROUP (1) osatumiza zithunzi kapena ma kanema olawula (2) osatumiza ma link ama group ena pamudzi pano (3) osatukwanizana pa group pano (4) kulemekeza maganizo anzathu ,sitingaganize mofanana (5) osatenga nkhani zokambidwa pano mwachisawawa chifukwa anthu akhala ndimaufula olankhula zakukhosi kwawo mosaopa (6) obwela ndichisokonezo sasowa ndipo sitizachedwa kum'panga remove (7) munthu Ali ndiufulu olemba kapena kugwiritsa ntchito mawu ake pogawana uthenga (8) osatumiza nkhani zabodza zopanda umboni pa group Kupezeka ophwanya malamulo adzachotsedwa pa group (9) Group la friends of makanjira liziyamikira kapena kudzudzula andale ,akapezeka munthu obweletsao chisokonezo pa group posafuna anthu kuti adzudzule kapena kuyamikira andale ,munthuyo adzachotsedwa pa group car h