TIKAMBE ZACHIKONDI
MALAMULO A MU TIKAMBE ZACHIKONDI
Takulandirani kuno ku Tikambe zachikondi
🪃🪃🪃🪃🪃🪃🪃🪃
ngati mwalowa kumene ponyani pic yanu ndikuliuza gulu dzina lanu ndi komwe mukukhala,
🌹🌹🌹🌹🌹
Timaletsa zinthu izi,ma sticker ,vn ,zithunzi zolaula ,ma link agulu lina, kunyozerana zipembedzo komaso mitundu
🐸🐸🐸🐸🐸
Kupedza wachikondi ndizololedwa muno ,koma za ku ibox zizithela komweko sisafike pagulupu
🌹🌹🌹🌹🌹
Monday to friday nthawi ikakwana 8 pm timakhala ndi topic, ndipo Sunday iliyonse ndi pic day
🌴🌴🌴🌴🌴
Ngati mulindinkhani ndipo mukufuna kuthandizidwa ,mpezeni admin wina aliyense ndikumpatsa nkhaniyo ku ibox ndipo nkhaniyanu izaponyedwa mosunga chinsisi
🪣🪣🪣🪣🪣
Z
Admin azatulutsa aliyense osatenga nawo gawo kugulupu kapena ophwanya malamulo
❤️❤️❤️❤️❤️
Satilani malamulo kuti mukhalitse muno
Zikomo.