𝐓𝐇𝐄 𝐏𝐑𝐄𝐒𝐄𝐍𝐓 𝐓𝐑𝐔𝐓𝐇 𝐆𝐑𝐎𝐔𝐏
Cibvumbulutso 14:6-10 Ndipo ndinaona mngelo wina alikuuluka pakati pa mlengalenga, wakukhala nao Uthenga Wabwino wosatha, aulalikire kwa iwo akukhala padziko, ndi kwa mtundu uti wonse ndi pfuko ndi manenedwe ndi anthu j ndi kunena ndi mau akuru, Opani Mulungu, mpatseni ulemerero; pakuti yafika nthawi ya ciweruziro cace; ndipo mlambireni iye amene analenga m'mwamba ndi mtunda ndi nyanja ndi akasupe amadzi, Ndipo anatsata mngelo wina mnzace ndi kunena, Wagwa, wagwa, Babulo waukuru umene unamwetsako mitundu yonse ku vinyo wa mkwiyo wa cigololo cace. Ndipo anawatsata mngelo wina, wacitatu, nanena ndi mau akuru, Ngati wina alambira ciromboco, ndi fane lace, nalandira lembapamphumi pace, pa dzanìI 6ja lace,𝐢𝐲𝐞𝐧𝐬𝐨 𝐚𝐝𝐳𝐚𝐦youth 𝐰𝐚𝐤𝐨 𝐤𝐮 𝐯𝐢𝐧𝐲𝐨 𝐰𝐚𝐦𝐤𝐰𝐢𝐲𝐨 𝐰𝐚 𝐌𝐮𝐥𝐮𝐧𝐠𝐮 𝐰𝐨𝐤𝐨𝐧𝐳𝐞𝐤𝐚 𝐰𝐨𝐬𝐚𝐧𝐠𝐚𝐧𝐢𝐳𝐚 𝐦𝐜𝐡𝐢𝐤𝐡𝐨 𝐜𝐚 𝐦𝐤𝐰𝐢𝐲𝐨 𝐰𝐚𝐜𝐞;𝐧𝐝𝐢𝐩𝐨 𝐚𝐝𝐳ďf𝐚𝐳𝐮𝐧𝐳𝐢𝐤𝐚 𝐧𝐝𝐢 𝐦𝐨𝐭𝐨 𝐧𝐝𝐢 𝐬𝐮𝐥𝐟𝐮𝐫𝐞 𝐩𝐚𝐦𝐚𝐬𝐨 𝐩𝐚 𝐚𝐧𝐠𝐞𝐥𝐨 𝐨𝐲𝐞𝐫𝐚 𝐦𝐭𝐢𝐦𝐚 𝐧𝐝𝐢𝐩𝐚𝐦𝐦 o𝐚𝐬𝐨 𝐩𝐚 𝐦𝐰𝐚𝐧𝐚𝐰𝐚𝐧𝐤𝐡𝐨𝐬𝐚