MRAKATULI WAPAPHATA, tigawane ndakatulo,nyimbo za pamalawi mwakathithi muno.
Welcome pa mrakatuli wapamphata;;;; chonde satilani izi kuti mukhalitse👇👇. 1, ngati mwalowa kumene khalani odekha chifukwa mutha kutulusidwa popopo, 2, mono zoponya zolaula ayi ukapezeka ulongeza kusadache, 3,cholinga cha group lino ndikupasana ndakatulo,komanso macheza,, 4,sitilola munthu kulo ku inbox Kwa mnzake opanda kupempha ukapezeka out. 5,ngati mwapeza vuto mu group ili aziwiseni addim ndipo akuthandizani. 6,anthu timapanga add loweluka lokha basi komanso ili nditsiku limenenso timabweresa chikolopa chosetsa onse ongofuna kuzadzitsa pa group pano 7,ngati mwakonda munthu mupempheni popa before kumulowera Ku inbox .. 8 loweluka lililonse tizikhala ndi pic day pachifukwa ichi aliyense akupemphedwa kutenga nawo gawo osateroyo out