๐จ๐จ GROUP LINO NDI LA SUPPORTERS WA BULLETS BASS NGATI ULI WA MA TEAM ENA TULUKANI KUNJA POMPANO, ๐ฆ๐น๐ฆ๐น MUNO TIMAKAMBIRA ZA MPIRA BASS,,๐ฏ ๐ฅ๐ฅ MA LINK MUNO AYI UKAPEDZEKA,,,๐น๐น ๐ฅ๐ฅ NKHANI ZA DZIPEMBEZO MUNO AYI UKAPEDZEKA ๐น๐น ๐ฅ๐ฅ UKAPEDZEKA UKUTUKWANA MUNO๐น๐น, ๐ฅ๐ฅ OSALOWERANA KU INBOX ๐ฅ UKAPEDZEKA ๐น ๐น ๐ฅ๐ฅ DZOLAULA (ma porn stickers)MUNO AYI UKAPEDZEKA ๐น๐น,, ๐ฅ๐ฅ WHOZA WHOZA MAULE,, ๐ฏ๐ฏZOPONYA MA CHANNEL MUNO AYI UKAPEDZEKA ๐น๐น ๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น MBAMBANDE MAULE ๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น ๐ฆ๐น๐ฆ๐น DZIKOMO ๐ฆ๐น๐ฆ๐น ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐๐๐๐๐๐๐๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*MALAMULO ATHU MUNO MU BULLETS MANOMA SILVER ๐ฅ ZAMASEWERO* โฝโฝโฝ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena ndi ma sticks ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* mphavu nyerere ๐๐๐๐๐ญ๐ณ๐ญ๐ณ๐ญ๐ณ๐ญ๐ณ mphavu bullets ๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น mphave silver ๐ฆ๐ท๐ฆ๐ท๐ฆ๐ท๐ฆ๐ท *umodzi pa machedza* ๐คธโโ๐คธโโ๐คธโโ๐คธโโ๐คธโโ
1๏ธโฃOsasitha chithuzi kapena mutu wa gulu 2โฃMa videos olaula muno ayi or pic. 3๏ธโฃOsatumiza link ya group lina muno ayinso 4๏ธโฃNo voice messages /stickers ๐ฏ. 5๏ธโฃMuno simosewela koma kugawana Sports ndi Tinkhani patali patali 6๏ธโฃkumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa. 7๏ธโฃUlemu kwa aliyese. 8๏ธโฃNkhan zaku inbox zithere Komweko. 9๏ธโฃNgati member wa group waona povuta pena pake pita kwa admin aliyese muuze kuti akuthandize ๐ Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi. 11. Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja ๐ *By Admin*
WELCOME TO FCB NYASA BIG 2๏ธโฃ0๏ธโฃ2๏ธโฃ5๏ธโฃ SUPPORTERS GROUP NDIPO MALAMULO ATHU ALI MOTEREโฌ๏ธโฌ๏ธโฌ๏ธ 1๏ธโฃ TIKONDANE WINA NDI MZAKE TOSE NDIFE BANJA LIMODZI MONGA MAPALE 2๏ธโฃOSAMASANKHANA MITINDU KAPENA CHIPEMBEZO 3๏ธโฃ NDI UDINDO WA WINA ALIYETSE KUTUMIDZA UPDATE PA GROUP PANO 4๏ธโฃ NO PORNO VIDEO OR PHOTO( ZITHUZ KAPENA MA VIDEO OLAURA MUNO AYI NDI ZOLETSEDWA 5๏ธโฃ OSAMAPONYA LINK YA GROUP LINA MUNO 6๏ธโฃ OSAMAPONYA MA STICKER MUNO 7๏ธโฃ NO VN MUNO POKHA POKHA ITAKHALA SPORTS 8๏ธโฃ WINA ALIYETSE AZITENGA MBALI MKAKHALA 1 WEEEK OSATENGA MBALI MZATULUSIDWA 9๏ธโฃ OSAMANYOZANA ๐ NKHAN ZA PA GROUP PANO ZIZIKHALA 90% ZA MPIRA MBALI INAYO TIKHOZA KUMACHEZALO DZINA 1๏ธโฃ1๏ธโฃ ZA NDALE MUNO AYI UKAPEZEKA REMOVE 1๏ธโฃ2๏ธโฃ NKHAN ZA GROUP PANO ZIZITHERA POMPANO NOT KU INBOX 1๏ธโฃ3๏ธโฃ MKAPEZA VUTO PITANI KU INBOX KWA ADMIN NDIPO TSATILAN MALAMULO ZIKOMO *BY ADMIN MUNSA ENTERTAINMENT ๐๐๐๐
A COLLECTION OF SEVENTH DAY ADVENTIST CHURCH HYMNS
*WELCOME TO ๐ ฑ๏ธ๐ ฑ๏ธ๐ฟ๐ฆ๐น FCB NYASA BIG BULLETS* *MALAMULO ATHU ALI MOTELE*๐๐๐ 1๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Tiyeni tikondane ngat banja limodzi* 2๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Muno kunyozana ayi ๐คชngat wina wapezeka akunyonza anzake remove ๐ฎโ๐๏ธ* 3๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Kuponya nkhani za masewelo si ntchito ya admin okha ayi ๐คkma aliyese* 4๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Za masewelo za kunja ngakhalenso kuno kwathu ndye zofunika koma zikhale zoona* 5๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Ngati mwalowelana ku inbox zithere komweko muno ayi* (koma osalowelana opanda chilorenzo ayi) 6๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Muno osaponya ma links agroup ina,Ukapezeka remove ๐ฎโ๐๏ธ* (sitilola maliki agrp ina) 7๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Muno aliyese osatenga mbali timamutulusa cox muno simongokhala chete ayi* (plus group ili sila asing'anga ai koma la mpira) 8๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *No VN, Porn videos, Stickers and ma photo alaula!* *Muno zonse tantchulazi sitilola Ukapezeka remove ๐ฎโ*๐ญ 9๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Zandale muno ayi, za chipembezo munso ayi, kutukwana ayinso๐ค ukapeza remove ๐ฎโ๐๏ธ* ๐๐ฟ๐ฆ๐น *Muno 95% ndi nkhani za bullets bas 5% osalayo ya ma team ena* 1๏ธโฃ1๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Kupanga left muno ndye kuti zampira simbali yako* 1๏ธโฃ2๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *KUTSOGONZA MULUNGU NDYE CHINTHU CHOPAMBANA KWABASI* 1๏ธโฃ3๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *GULU LIZINKHALA LOSEKA KUYAMBIRA 10:30pm FOR SECURITY REASONS MALINGA NDI ANZATHU OFUNA KUTUMIZA ZOSAYENERA* *๐ฐ๐By your Administration* *Ngati mwalikonda group ili, tsatilan malamulo onsewa kuti tikhale limodzi bye bye for now* Don't forget (We are here for the football) *FOREVER MAULE ๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฟ๐ฟ๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฅ๐ฅ*
Malamulo aa group ali mothelo 1 Vn yoletsedwa โโ 2 macheza katiti โ โ 3 Voice chat yoletsedwa โโ 4 kutukwanana muno ay โโ 5 Nkhani za mpira โ โ โ 6 ma stick No โโ 7 mautenga okuza team ina ay โโ 8 ma link aa group lina ay โ โ 9 Lamulo lomaliza chonde mokumbepa all members monga masapoter aa team yathu ya NBB NYASA BIG BULLETS chonde osanyosa ma admin tikale okondana kulakwisa admin timausana kut tikotse mvuto limenelo zikomo maule notse ๐๐๐๐๐