CommunitiesIMVAN KHANI KUZELA KWA IFE MWACHANGU

IMVAN KHANI KUZELA KWA IFE MWACHANGU

600+ membersActive this monthKMB

About this community

MALAMULO NDI AWA NGATI MWALOWA KUMENE MUMVE MUTIMAMO KUTI MWALANDILIDWA KHALAN OMASUKA...... GROUP INO IMAPANGA DZA KHANI ILIYOSE IMENE INGAPEZKE TIMAPONYA FULL TIME MA UPDATE TIZIKUPASILANI BAS GROUP INO NSITISEGULA AI TIMANGOPNYAP DZITHU INUYO MUZINGOWELENGA BAS CHOMWE MUNGAZIWE INUYO NDINE NDI ATHU AMENE TINGA PITISE CHISOGOLO..... KUPONYA LINKS YATHU NDIKWA ALIYESE 🔙

AIKMB
Unlock / View Community

Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.

Related communities

KHANI🔥🔥 ZAKUCHIPINDA🔥🔥 AND🔥🔥 MACHEZA🔥🔥 GULUPU

*TAKULANDILANI KUGULUPU LATHU LA KHANI ZAKUCHIPINDA MOTSOGOZEBWA NDINE F KHOZA KAPENA KUTI FRANK KHOZA NYAMATA WAPA MWAZA NDIPO KHALANI OMASUKA CHOLINGA CHA GULUPU LATHU NDIKUFUNA KUPHUZITSANA NDI KUDZIWANA* 1️⃣ *NDIPO MALAMULO ATHU ALI MOTELE NGATI MWALOWA KUMENE MUKUYENELA KUPONYA PIK KOMASO DZINA NDI KOMWE MUKUKHLA* 2️⃣ *KUPONYA MA VIDEO NDIKWAWIMA ALIYESE OSADIKILA ADAMN OKHA* 3️⃣ *KULOWA KU IN BOX KWAMUTHU OPANDA CHILOLEZO* ❌❌❌❌❌❌❌❌ 4️⃣ *KUNYOZANA KAPENA KUTUKWANIZANA SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA*❌❌❌❌❌❌ 5️⃣ *MA Link AMA GULUPU ENA SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA* ❌❌❌❌❌❌ 6️⃣ *MA VN SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA* ❌❌❌❌❌❌❌❌ 7️⃣ *MA STICKER SITIMALOLA MUKAPEZEKA* ❌❌❌❌❌❌❌ 8️⃣ *NGATI SIMUKUTENGA MBALI PAMA PROGRAM ATHU MUDZATULUTSIBW 9️⃣ *KUTUMIZA MA VIDEO NDIKWAWIMA ALIYESE OSADIKILA ADAMN OKHA* 🔟 🎄🎄🎄🎄🎄 *Dzina la hule muno sitimalola ukapezeka panja*

1K+ membersNYA

ZBS KUTHYAKULA NKHANI

1 Osasitha chithunzi kapena mutu wa gulu ❌❌❌❌ 2 Ma videos olaula or pic muno ayiii..🚫🚫🚫🚫❌❌❌❌ 3 Osatumiza link ya group lina muno ❌❌❌❌❌ 4 No voice messages/ stickers.❌❌❌❌ 5 Muno simosewela komo kugawana NKhani ndi Sports.✅ 6 Kumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa.✅ 7 Ulemu kwa aliyese ndiofunika✅ 8 Nkhani zaku inbox zithere Komweko Osazibweretsa Pano✅ 9 Ngati member wa group waona polakwika alowe ku inbox kwa admin Kuti Amthandize✅ 10 Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi.🚫🚫🚫❌❌❌❌❌❌ 11 Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja.✅ 🔚 by Admin

800+ membersCJK

MA LINK, MA SCANDAL NDI NKHANI

*MWALANDIRIDWA MUNO NONSE.* *MALAMULO AMUNO ALI CHONCHI:* *1. Osanyozana kapena kunyozana mtundu kapena chipembedzo.* *2. Osaponya link imodzi mobwereza, muzidikira ma hours angapo mkuponyanso.* *3. Osatsatsa malondamuno. Ma porno ayi muno.* *4. A Sing’anga muno ayi.* *5. Za ma status zizithera ku ma status komweko.* *6. Ma Gif kapena stickers muno ayi*

700+ membersFUF

ZBS KUTHYAKULA NKHANI

1 Osasitha chithunzi kapena mutu wa gulu ❌❌❌❌ 2 Ma videos olaula or pic muno ayiii..🚫🚫🚫🚫❌❌❌❌ 3 Osatumiza link ya group lina muno ❌❌❌❌❌ 4 No voice messages/ stickers.❌❌❌❌ 5 Muno simosewela komo kugawana NKhani ndi Sports.✅ 6 Kumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa.✅ 7 Ulemu kwa aliyese ndiofunika✅ 8 Nkhani zaku inbox zithere Komweko Osazibweretsa Pano✅ 9 Ngati member wa group waona polakwika alowe ku inbox kwa admin Kuti Amthandize✅ 10 Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi.🚫🚫🚫❌❌❌❌❌❌ 11 Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja.✅ 🔚 by Admin

500+ membersCJK

KHANI ZA KUCHIPINDA TICHEZE MWAKATHITI💥💥

TAKULANDILANI KU KHANI ZA KU CHIPINDA KARANI OMASUKA 🤸🏼🤸🏼‍♂️🅱️❓❓❓

500+ membersYAO

ZOCHITIKA MU AFRICA PANO PA CHINYANJA SERVICE NO FAVOUR NO FEAR KOMA KUKUPASILANI NKHANI ZOKHA ZOKHA

1 Osasitha chithunzi kapena mutu wa gulu ❌❌❌❌ 2 Ma videos olaula or pic muno ayiii..🚫🚫🚫🚫❌❌❌❌ 3 Osatumiza link ya group lina muno ❌❌❌❌❌ 4 No voice messages/ stickers.❌❌❌❌ 5 Muno simosewela koma kugawana NKhani ndi Sports.✅ 6 Kumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa.✅ 7 Ulemu kwa aliyese ndiofunika✅ 8 Nkhani zaku inbox zithere Komweko Osazibweretsa Pano✅ 9 Ngati member wa group waona polakwika alowe ku inbox kwa admin Kuti Amthandize✅ 10 Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi.🚫🚫🚫❌❌❌❌❌❌ 11 Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja.✅ 🔚 by Admin

400+ membersNYA

Related searches

AI WhatsApp communitiesBrowse all communities