Communities🎼KUSIFU NA KUABUDU KWA NYIMBO ZA KIKATOLIKI 🎹

🎼KUSIFU NA KUABUDU KWA NYIMBO ZA KIKATOLIKI 🎹

200+ membersSWH

About this community

Anayeruhusiwa kuwa humu ni Mkristo Mkatoliki yeyote ambaye anapenda kwaya na kuimba, anayependa nyimbo zetu sio mpaka yeye awe mwanakwaya ilimradi apende kusikia nyimbo (Mara chache anaweza kuwa dhehebu jingine yaweza asiwe Mkatoliki ila awe Mkristo na anapenda nyimbo za Wakatoliki na uimbaji wa Katoliki hata kama anapenda na za upande wakwake ila awe pia na huku anapenda) ->Malengo makuu ni:- 👉Kushare links za nyimbo mbalimbali za Kikatoliki za kwaya zetu. 👉🏾Kushare ujuzi mbalimbali kuhusu uimbaji Katoliki. 👉🏾Kupeana taarifa mbalimbali za kuhusu uimbaji na kimaisha. 👉🏾Kutangaza biashara zinazohusu muziki mtakafifu na kuboresha uimbaji 👉🏾Kuburudishana kupitia clips na meme mbalimbal za kiuimbaji (Tutaendelea kuboresha kadiri ya muda)🙏🏽

SWH
Unlock / View Community

Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.

Related communities

NYIMBO NDI MACHEZA ALL WELCOME 💃🏽🕺🏽💃🏽🕺🏽

*WELCOME TO NYIMBO NDI MACHEZA*🎶🎵💃🏼🕺🏻💃🏼🕺🏻❤️❤️ *MALAMULO⤵️* *(1)Mukalowa ponyani chithuzi/photo yanu ndikumene mukukhalira. Komanso kumatengapo mbari muzochitika zathu osangokhara chete🧎🏻* *(2)Kunyozerana zipembedzo/kunyozana wina ndi mzake sizoloredwa ukapezeka remove.*❌❌❌ *(3)Sitimalora kulankhula, nkhani, zithuzi or ma videos olawura/porno, ukapezeka remove*❌❌❌ *(4)Kutumiza ma audio/VN, stickers AYI ukapezeka remove.*❌❌❌ *(5)Ndi udindo wa aliyense kutumiza nyimbo, mukamatumiza onetsetsani kuti ndi document. Za ma video kumalemba woyimba ndi tittle kupanda kutero remove🎶*❌❌❌ *(6)Sizololedwa kulowerana ku inbox koma ngati mwagwirizana kuti muzicheza ku inbox ndi ufulu wanu komanso ngati mukuwona Kuti mukuvutitsidwa kwambiri muli ndi ufulu kuwuza admin zankhaniyi.* *(7) Ngati munthu wakulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and sizinaku sangalatseni osabweretsa nkhani pa group, mudzatulutsidwa chifukwa zima bweretsa chisokonezo pa group, pitani ku inbox kwa admins adzakuthandizanj.* *(8) Sunday tidzikhara tikuponya chithuzi/pic day kupanda kuponyanawo remove*❌❌❌ *(9)Ndikoletsedwa kuponya ma links amagroups ena komanso a facebook ndi YouTube ukapezeka remove.* *(10) Musana pemphe zondani kaye wanthu pa group pano chikhalidwe or MUSADABWE NYIMBO yanu ikapanda kupatsidwa. Chikhalidwe ndichofunika.* *(11) Zandale muno, mpira kapena kunyoza chipembedzo komanso za malonda kapena a sing’anga sizoloredwa or remove*❌❌ *(12) Nyimbo zonse zizi pemphedwa pano osati ku inbox or mudzatulutsidwa* *(13) Chilankhulo muno ndi Chichewa ndi Chizungu basi.* *(14) Ngati member wa kulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and simuna sangalare nanzo wunzani admin straight osadikira kuti pathe week/ma week chifukwa zimabvuta kupanga sort out nkhaniyo komanso muzibweretsa ndi umboni kwa admins kuti admins athe kuyendetsa nkhani yo bwino.* *(15)Tiyeni titsatire malamuro tonse Kuti nthawi ndimatsiku okhala muno achuluke* *KHALANI OMASUKA KOMANSO KUTENGAPO MBALI MU ZOCHITIKA ZATHU* *By admin* 💃🏽🕺🏽❤️

900+ membersNYA

SDA NYIMBO ZA UZIMU GROUP 1

*NYIMBO ZOTAMANDA KOMANSO KUKWEZA YEHOVA*

800+ membersKNG

KALE LANGA (NYIMBO, ...)💃🏻

Malamulo a Muno ------------------------------ (1)Kupempha ndikutumiza nyimbo. (2)Nyimbo zake ziyambire 2010 kumatsika kumusi. (3)Osatukwanana wina ndimzake timalimbikitsa ubale muno. (4) Osatumiza link or ma Photo olaura kapenanso zosemphana ndi group lino muzachotsedwa. (5)Osanyozerana mtundu kapena chipembedzo tonse ndi amodzi. Komaso osaponya ma sticker muno ayi (6)Ndi udindo wa aliyense kutumiza ndikupempha nyimbo zakale koma ngati mwafuna zatsopano pemphani ku inbox ena azakupatsani komweko. (7) Ma voice note siololedwa muno koma zikavutitsitsa kuti mufuna nyimbo nde mutu wake simukuudziwa funsani admin aliyense kuti mumumvetseletse Voice note ndipo akusakireni . (8)Osatukwana muno tili ndi anthu akulu akulu azaka zapakanthawi omwe amafunika kuwalemekeza. Tiyeni titsate malamuro kuti tipitilize kusangalara ndinyimbo komanso zochitika zotikumbutsa kale lathu .

700+ membersYAO

KUGAWANA NYIMBO MWAKATHITHI 🔥🔥

*WELCOME TO KUGAWANA NYIMBO MWAKATHITHI*. 🫂🎧🎧🎼🎵🎵🎶 *MALAMULO ATHU ALIMOTELE👇🏼👇🏼*. *1.🛑ukangojoina kumene group yambakaye waponya pic... Yako ndikuzilongotsola dzina lako ndikomwe ukuchokera*. *2.🛑Tilemekedzane wina ndinzache posatengera mtundu kapena chipembedzo or kochokera*.❌❌⛔📛🚫 *3.🛑No ma videos kapena zithunzi zolawula muno even ma voice notes❌❌⛔📛🚫ukangopedzeka remove🎬🚮*. *4.🛑No any foreigner groups/links, ma short videos or stickers muno ayi❌❌⛔📛🚫ukangotumidza basi uwona nsana wanjira🎬🚮*. *5.🛑ndiudindo wawina aliyense otumidza nyimbo muno osamangodikira ma admin okha kuti atumidze nyimbo❌❌⛔📛🚫*. *6. 🛑Then usanapemphe nyimbo yamba kaye waponya nyimbo zomwe iwe ulinazo ndipo ife tizakuthandidza the same time*. *7.🛑Kupempha mowirikidza koma iwe osatumidza zimenezo ayinso❌❌⛔📛🚫ma camera akakuwona 👀basi remove ndiyomweyo🎬🚮*. *8.🛑Ndipo osatenga nawo gawo pa maprograms amenewa timasazikana naye mosayang'ana nkhope🤣❌❌⛔📛🎬🚮*. *⚠️🚸WARNING: ngati wapedza kt group lakiyidwa🔐🔐🔒🔒osafunsa kt why?❌❌⛔📛 Udzalandira remove 🎬🚮ndekuti ma admin akukonza zina zake zosemphana ndi group*. *#. ✅✅Tsatilani zimenezi kt matsiku anu okhala muno achuluke musanawone nsana wanjira ngati omwe adawona John chilembwe kumandala😉*. *#. ✅✅Machedza wez koma nyimbo kathithi...*. *WROTE BY ALL ADMINISTRATOR OFFICCERS, MWAKOMA NONSE🥳🥳💃🏻💃🏻🤼‍♀️🤸🏻‍♀️🤸🏻🏋🏻‍♀️🙊🙌🏻🙌🏻*.

500+ membersActive this monthYAO

KUCHIMAKE KWA NYIMBO KATHITHI⏭️🎶🎶🎶

TAKULANDIRANI KUNO KUCHIMAKE KWA NYIMBO KANTHITHI MARAMURO ALI MOTERE👇👇 (1). Osatumiza link ya group Lina  muno (2). Muno ma voice recording ayi aliyense akuyenera kulemba basi (3) kutumiza ma vedio kapena zithunzi zolawura muno ayi (4) Ukaponya nyimbo kapena vedio ukuyenera kulemba title ndamene anayimba (5)  kulemba title zimathandiza munthu kut usatenge nyimbo yomwe uli nayo kale (6)  Zosakhana mitundu muno ayi tonse ndife amodzi, nkhani za mipingo, ndale  ndi mpira muno ayi BY ADMIN ✍️✍️✍️✍️✍️. .......

500+ membersSWH

NYIMBO NDI MACHEZA ONE (MUSIC AND CHATS) ALL WELCOME 💃🏽🕺🏽💃🏽🕺🏽 ❤️❤️

*WELCOME TO NYIMBO NDI MACHEZA ONE (MUSIC AND CHATS)*🎶🎵💃🏼🕺🏻💃🏼🕺🏻❤️❤️ *MALAMULO⤵️* *(1)Mukalowa ponyani chithuzi/photo yanu ndikumene mukukhalira. Komanso kumatengapo mbari muzochitika zathu osangokhara chete🧎🏻* *(2)Kunyozerana zipembedzo/kunyozana wina ndi mzake sizoloredwa ukapezeka remove.*❌❌❌ *(3)Sitimalora kulankhula, nkhani, zithuzi or ma videos olawura/porno, ukapezeka remove*❌❌❌ *(4)Kutumiza ma audio/VN, stickers AYI ukapezeka remove.*❌❌❌ *(5)Ndi udindo wa aliyense kutumiza nyimbo, mukamatumiza onetsetsani kuti ndi document. Za ma video kumalemba woyimba ndi tittle kupanda kutero remove🎶*❌❌❌ *(6)Sizololedwa kulowerana ku inbox koma ngati mwagwirizana kuti muzicheza ku inbox ndi ufulu wanu komanso ngati mukuwona Kuti mukuvutitsidwa kwambiri muli ndi ufulu kuwuza admin zankhaniyi.* *(7) Ngati munthu wakulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and sizinaku sangalatseni osabweretsa nkhani pa group, mudzatulutsidwa chifukwa zima bweretsa chisokonezo pa group, pitani ku inbox kwa admins adzakuthandizanj.* *(8) Sunday tidzikhara tikuponya chithuzi/pic day kupanda kuponyanawo remove*❌❌❌ *(9)Ndikoletsedwa kuponya ma links amagroups ena komanso a facebook ndi YouTube ukapezeka remove.* *(10) Musana pemphe zondani kaye wanthu pa group pano chikhalidwe or MUSADABWE NYIMBO yanu ikapanda kupatsidwa. Chikhalidwe ndichofunika.* *(11) Zandale, mpira kapena kunyoza chipembedzo komanso za malonda kapena a sing’anga sizoloredwa or remove*❌❌ *(12) Nyimbo zonse zizi pemphedwa pano osati ku inbox or mudzatulutsidwa* *(13) Chilankhulo muno ndi Chichewa ndi Chizungu basi.* *(14) Ngati member wa kulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and simuna sangalare nanzo wunzani admin straight osadikira kuti pathe week/ma week chifukwa zimabvuta kupanga sort out nkhaniyo komanso muzibweretsa ndi umboni kwa admins kuti admins athe kuyendetsa nkhani yo bwino.* *(15)Tiyeni titsatire malamuro tonse Kuti nthawi ndimatsiku okhala muno achuluke* *KHALANI OMASUKA KOMANSO KUTENGAPO MBALI MU ZOCHITIKA ZATHU* *By admin* 💃🏽🕺🏽❤️

400+ membersNYA