CommunitiesMachilitso oona ali m'chilengedwe

Machilitso oona ali m'chilengedwe

200+ membersNYA

About this community

MALAMULO A GROUP INO ALI MOTELEπŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡ Khalani omasuku pofusa mafuso kut muthandizidwe moyenela. Ngat nthenda yomwe mukufuna kufusa simukudziwa dzinalake fotokozani zizindikilo zake kuti tiizindikile mosavuta nkukuthandizani. Nkhan Zokhuza zinsisizanu zifusani ku inbox kut muthandizidwe mwachinsisi. Chilichonse chomwe sichikukhuzana ndi mafuso kapena mayankho pa zitsamba ncholesedwa mukapezeka pompo REMOVE/MUZATULUSIDWA. Kuyambisa macheza omwe ena atha kukhumudwapo kapena ndi cholinga chowa chepsa nkolesedwa mukapezeka pompo MUZATULUSIDWA/REMOVE. GULULI NDI LOLIPILA ndrama yokwana K250 PAMWEZI_____ member aliyense azayenela kulipila mwez ulionse popanda kutelo MUZATULUSIDWA/REMOVE. Ndrama imenei izathandiza ADMIN kut asamasowe pa group pano chifukwa chosowa bundle komaso azitha kutiyankha komaso kupeleka matopic mwapafupipafupi munthawi yake. Ngat mwalipila fee yanu chonde nenani ku inbox kut akuikeni mu gulu la anthu omwe satulusidwa mwez umeneo πŸ™πŸ™ KWA ALENDO TONSE πŸ‘¨β€πŸ¦ΌπŸ‘¨β€πŸ¦ΌπŸ‘¨β€πŸ¦ΌπŸšΆβ€β™€οΈπŸšΆβ€β™€οΈπŸšΆβ€β™€οΈπŸšΆβ€β™‚οΈ tizipasidwa sabata/ week imodzi yatunthu yaulele tikatelo tiziyenela kulipila fee yapamweziyi ngat takonda kukhala, ngat sidalikonde gululi tikangotha week tikuyenela kutuluka tokha(LEFT ) tisawapase admin ntchito yotitulusa. Ngat mwatulusidwa ndipo mukufuna kulowaso lipilani fee ndikunena ku inboxπŸ™πŸ™ Ma number omwe Tizilipilako fee yathu ndi awawaπŸ‘‡πŸ‘‡ [contact hidden] (THOMAS STANFORD JOHN) Gao lililonse lokhuza kumanga kapena kumasula/kupasula banja musafuse pano koma ku inbox (❓(panoso pali ena ndi mabanja).πŸ™πŸ™ Gao lililonse lokhuza chinsisichanu musafuse pano koma ku inbox. ALIYENSE SAKULOLEDWA KULANKHULA/KUFUSA PA VOICE NOTE POKHA POKHA NGAT NDINU ADMIN MUKAPEZEKA POMPO MUZATULUSIDWA‼️ Khalani ndichidwi ndi ma voice note chifukwa mayankho ku matopic onse azipelekedwa pa voice note πŸ™πŸ™ ngati mayina amitengo omwe atchulidwa mu voice note simukuwadziwa onesetsani zithuzi za mitengo yatchulidwayo kut muizindikileπŸ™πŸ™ Za mavuto anu lowani ku inbox πŸ‘‰0995334373

NYA
Unlock / View Community

Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.

Related communities

CHOONAD CHAKUMAPETO 3️⃣

*YAHUSHA anati Kwa iye ine ndine kuuka NDI moyo yense okhulupilila ine angakhale amwalila azakhalaso NDI moyo Yohane 11:25*

800+ membersNYA

ZACHILENGEDWE ZIMACHILISA πŸ₯¬πŸ₯¦πŸŒ³πŸƒ

Welcom all members Group rules Pangani zogwilizana ndi group zokhuza makhwala zokha No vn No videos No kuyankhula zosephana ndi cholinga cha group Muno chilichose timaphunzisa komaso kupereka komwe muli or kubwera kunoko kumitambo. Nkharani omasuka , funsani zomwe mukufuna kut tikuthandizeni. Participating is the must ngat munthu Akhara 1 week osafunsako or kuyankhulako kalikose timachosa . Muno si zoti munthu azitenga ma information amuno ndikukatuma kwina nooo if so tizapanga remove Ndipo muno chilichose nchaulele.🎩🎩🎩🌲🌳🍜🍲

600+ membersKDE

πŸ“–MaTalasimu Ndi makhwala Achoonadi

Kwaomwe mukufuna kuthandizidwa bwelani ku in box ndikuzifotokoza Komaso ndikomwe muli ziwani kuti makhwala a maTalasimu sizitengela chipebezo cha Muthu wina aliyese athandizidwe moyenelelaπŸ‘

600+ membersFUF

CHOONAD CHA KUMAPETO 1️⃣

*YAHUSHA anati Kwa iye ine ndine kuuka NDI moyo yense okhulupilila ine angakhale amwalila azakhalaso NDI moyo Yohane 11: 25*

500+ membersNYA

LPM YOONA | NO HIDETAG

Seperti lpm pada umumnya. [link hidden β€” subscribe to view]?mode=gi_t

400+ membersWAR

YESU NDiYE NJILA CHOONADI NDI MOYOπŸ“–πŸ“–πŸ“–

[link hidden β€” subscribe to view]

300+ membersLUA