Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
MALAMULO ππΌππΌ 1. Mukalowa tchulani dzina ndi komwe mumakhala kuti anthu akudziweni. 2. Zolaula muno ayi. 3. Nkhani za ku inbox zizithela komweko. 4. Osanyozelana Zipembedzo. 5. Tikuyenela kulemekezana wina ndi mzake. 6. Tiziponya nkhani zoona zokhazokha. 7. Mukafuna kulowa gulu la zachifundo fikilani admin kuti akulongosoleleni bwinobwino. 8. Ngati mwalakwilidwa afikileni adindo kuti akuthandizeni. 9. Aliyense akupemphedwa kutenga gawo muzochitika. 10. Nthawi yophunzitsana chinthu tikupemphedwa kutsatila mwachidwi ndi ndemanga komanso ngati sitikumvetsa tizifunsa pamapeto pa phunziro. 11. Ma stickers komanso ma vn ndi oletsedwa. 12. Za asing'anga komanso ma link ena ndi oletsedwa.
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
1 Osasitha chithunzi kapena mutu wa gulu ββββ 2 Ma videos olaula or pic muno ayiii..π«π«π«π«ββββ 3 Osatumiza link ya group lina muno βββββ 4 No voice messages/ stickers.ββββ 5 Muno simosewela komo kugawana NKhani ndi Sports.β 6 Kumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa.β 7 Ulemu kwa aliyese ndiofunikaβ 8 Nkhani zaku inbox zithere Komweko Osazibweretsa Panoβ 9 Ngati member wa group waona polakwika alowe ku inbox kwa admin Kuti Amthandizeβ 10 Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi.π«π«π«ββββββ 11 Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja.β π by Admin