Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
TAKULANDILAN ALENDO MUNO PEZANI WACHIKNDl WANU Lemekezani malamulo ππ 1 Ukalowa ponya PIC ndikomwe umakhala 2 Ukafuna kucheza ndimkazi ku inbox uza ky admin 3 Osaponya ma Link a group yina β 4 Audio or VN Ayi 5 muno ukapezeka ukulemba English β 6 Ndiufulu waliyese kuponya mapono 7 Ngat sukutengapo mbali pa nkhani zose β 8 Ngat ndi Stick yapono utha kuponya 9 Tsiku laTopic ndi limodz lachiwir madzulo kuyamba 7 o'clock 10 Tikhale okondana kuti group la2 lipite patsogolo 11 Oyambitsa voice chat join limove β Lemekezan malamulo kuti masiku amuno achuluke
WELENGANI MUSANAPANGE JOIN PLEASE : NTCHITO YA ADIMINπ₯π₯π₯π₯πππ CHOLINGA CHA GULU LINO KUDZIWITSA MOMWE AKUTULUKILA MA FLIM A CHICHEWA KWA ONSE AMAWAFUNA. TIMADZIWITSA POTUMIZA KWA MA CUSTOMER ATHU IZI 1..Entertainment π₯π₯ 2..part imodzi ya filimπ₯π₯ 3..Poster ya filimπ₯π₯ 4..Nthawi yomwe yatuluka filim timapanga screenshot π₯π₯ 5..Nthawi yomwe tatumizila pa VIP timapanga screenshot π₯π₯ DZIWANI KUT MUKALIPILA KAMODZI MUZILANDILA MA FILIM PA V.I.Pπ₯π₯ TSIKU LILILONSE PA WEEK KOMANSO PA MWEZI MOSAVUTA MUNTHAWI YAKE YOMWE YATULUKILA FILIM. Talk TO ME INBOX CHAT WHILE I'M ONLINEπ₯π₯. NDIYANKHULEN KU INBOX NDILI ONLINEπ₯π₯. ZIKOMO. [link hidden β subscribe to view]
πΎππ₯¬πΏπ΄Timaphuzisana zamakhwala plus zachikondi, tikhani pang'ono tingazisamale bwanji pa moyo wathu.π₯³π₯³πΏππ₯¬πΎ timasukilane zambanjaπππ
TAKULANDILANI PANO PA KUPEZA WACHIKONDI MOSAVUTA AND MOSALIPILITSA Malamulo ali motere 1οΈβ£ kupeza wachikondi ndi ulere 2οΈβ£ ngt mukufuna mkazi /mamuna pezani admin aliyese ndipo muzifotokoze like 1 zaka 2 ana ngt mulinao 3 mukukhala kt nanga wachikondiyo akhale wakt 4 akhale wazaka zingt mkazi/mamuna mukumufunayo mukatelo muzidikila admin mwamutumizila zithuyo kubwereselani wachikoniyo 3οΈβ£ ngt mkazi or mamuna mwapatsidwao sadakusangalaseni muliso ndi mwai obwera kwa admin ndikuwauza kt akupaseniso wina 4οΈβ£ sitimalora zinthu izi 1 kuzipanga post wekha 2 ndi admin ekhayo amapanga post muthu ngt mwini wakewe ukuvomera kt akupange post pa grp 5οΈβ£ ngt mwalowa ku inbox kwa mkazi ky mamuna without admin zomwe mukazione uko ife sizimatikhudza 6οΈβ£ timakhala ndi call pa grp pano aliyese ndioloredwe kukapanga join 7οΈβ£ pano sitimalora zinthu izi 1 Zolaula 2 ma sticker 3 kunyozana 4 link ya grp ina muno ai 5 za ku inbox ky maudani akomwetimakhalako asabwere pano Ngt zina zakusowetsa mtendereukufuna ma ganizo anthu pezani admin tizapnga topic ndipo muzapeza choonadi kuchokera ku maganizo anthu omwe amapeleka pa toic Akapezeka onyozela malamulowa timapanga remove posatengera mtundu By admin