TAKULANDILANI PANO PA KUPEZA WACHIKONDI MOSAVUTA AND MOSALIPILITSA Malamulo ali motere 1️⃣ kupeza wachikondi ndi ulere 2️⃣ ngt mukufuna mkazi /mamuna pezani admin aliyese ndipo muzifotokoze like 1 zaka 2 ana ngt mulinao 3 mukukhala kt nanga wachikondiyo akhale wakt 4 akhale wazaka zingt mkazi/mamuna mukumufunayo mukatelo muzidikila admin mwamutumizila zithuyo kubwereselani wachikoniyo 3️⃣ ngt mkazi or mamuna mwapatsidwao sadakusangalaseni muliso ndi mwai obwera kwa admin ndikuwauza kt akupaseniso wina 4️⃣ sitimalora zinthu izi 1 kuzipanga post wekha 2 ndi admin ekhayo amapanga post muthu ngt mwini wakewe ukuvomera kt akupange post pa grp 5️⃣ ngt mwalowa ku inbox kwa mkazi ky mamuna without admin zomwe mukazione uko ife sizimatikhudza 6️⃣ timakhala ndi call pa grp pano aliyese ndioloredwe kukapanga join 7️⃣ pano sitimalora zinthu izi 1 Zolaula 2 ma sticker 3 kunyozana 4 link ya grp ina muno ai 5 za ku inbox ky maudani akomwetimakhalako asabwere pano Ngt zina zakusowetsa mtendereukufuna ma ganizo anthu pezani admin tizapnga topic ndipo muzapeza choonadi kuchokera ku maganizo anthu omwe amapeleka pa toic Akapezeka onyozela malamulowa timapanga remove posatengera mtundu By admin
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*TAKULANDIRANI KU TIPEZE WACHIKONDI 💓💓* *MALAMURO NDI AWA* 👇 *1️⃣ALIYENSE AKUYENERA KUTENGA NAWO MBALI KUTI MACHEZA AKOME KOMASO KUTI TIPEZE WACHIKONDI MOSAVUTA👩❤️💋👨👨❤️👨* *2️⃣MULENDO UKAFIKA AKUYENERA KUPONYA PIC NDI KUNENA KOMWE UMAKHALA💃🕺* 🤳 *3️⃣MA LINK AMA GROUP ENA MUNO AI 👺👺* 4️⃣ *MA PROGRAM ATHU ALI MOTERE:* *MONDAY, WEDNESDAY NDI FRIDAY TIMAKHALA NDI* *TOPIC. NDIPO SUNDAY NDI PIC DAY* 💃🕺🤳 *5️⃣NKHANI ZA KU INBOX ZIZITHERO KUMWEKO* 🫐🫐🫐🫐🫐 *6️⃣KUCHEZERANA KUZIWANA KUMAONONGA GROUP KUMACHEZA NDI ALIYENSE* 🤺 *7️⃣VOICE NOTE MUNO AI & WEEK ILIYONSE TIMACHOSA ANTHU OSATENGA NAWO MBALI* 🤺🏹 *🌹🌹🌹TIPEZE WACHIKONDI*
Timapereka ngongole za business komanso Ulimi
TAKULANDILAN ALENDO MUNO PEZANI WACHIKNDl WANU Lemekezani malamulo 👇👇 1 Ukalowa ponya PIC ndikomwe umakhala 2 Ukafuna kucheza ndimkazi ku inbox uza ky admin 3 Osaponya ma Link a group yina ❌ 4 Audio or VN Ayi 5 muno ukapezeka ukulemba English ❌ 6 Ndiufulu waliyese kuponya mapono 7 Ngat sukutengapo mbali pa nkhani zose ❌ 8 Ngat ndi Stick yapono utha kuponya 9 Tsiku laTopic ndi limodz lachiwir madzulo kuyamba 7 o'clock 10 Tikhale okondana kuti group la2 lipite patsogolo 11 Oyambitsa voice chat join limove ❌ Lemekezan malamulo kuti masiku amuno achuluke
*Kodi mwakhala mukusakasaka mpamba wa business komanso ulimi koma osaupeza?? Mwai wanu tsopano wapezeka ndi Bungwe la poverty eradication initiative lomwe limapereka ngongole za business komanso ulimi Kwa amalawi onse*
WELENGANI MUSANAPANGE JOIN PLEASE : NTCHITO YA ADIMIN🔥🔥🔥🔥👇👇👇 CHOLINGA CHA GULU LINO KUDZIWITSA MOMWE AKUTULUKILA MA FLIM A CHICHEWA KWA ONSE AMAWAFUNA. TIMADZIWITSA POTUMIZA KWA MA CUSTOMER ATHU IZI 1..Entertainment 🔥🔥 2..part imodzi ya filim🔥🔥 3..Poster ya filim🔥🔥 4..Nthawi yomwe yatuluka filim timapanga screenshot 🔥🔥 5..Nthawi yomwe tatumizila pa VIP timapanga screenshot 🔥🔥 DZIWANI KUT MUKALIPILA KAMODZI MUZILANDILA MA FILIM PA V.I.P🔥🔥 TSIKU LILILONSE PA WEEK KOMANSO PA MWEZI MOSAVUTA MUNTHAWI YAKE YOMWE YATULUKILA FILIM. Talk TO ME INBOX CHAT WHILE I'M ONLINE🔥🔥. NDIYANKHULEN KU INBOX NDILI ONLINE🔥🔥. ZIKOMO. [link hidden — subscribe to view]
🌾🎋🥬🌿🌴Timaphuzisana zamakhwala plus zachikondi, tikhani pang'ono tingazisamale bwanji pa moyo wathu.🥳🥳🌿🎋🥬🌾 timasukilane zambanja🍆🍌🍎