WELLCOME TO KUPHWETSA MKUTO PA PHWETTE LA MACHEZA GROUPโโ๐๐ฃ๐ค๐ช* *~_NGATI ULI SING'ANGA ZIPASILETU ULEMU SOCIAL MEDIA SIMAOPA MAULA_~* *๐Cholinga cha group lino ndikundikulimbikitsa ubale komaso macheza pajaamati kuyendamkumvina๐ค๐ค๐ช* *MALAMULO ATHU ALIMOTELE๐๐๐๐๐* *1๐Osatumiza link ya group ina muno opezeka remv๐ซ* *2๐Mulendo akalowa ayenera kuponya pic komaso kunena komwe amakhala โ * *3๐ma VN ( RECORD โบ๏ธ) muno ayi* *4๐Tiyenela kulemekezana wina ndizake osati kusalana* *5๐sunday llililose tixikhala ndi pic day โ * *6๐Ngat mwalowelana ku inbox zizithera komweko zisafike kuno* *7๐osaponya zithuz zolaula komaso ma vidios olaula* *8๐Ma mumbers nose ndinu ololedwa kubwela ndi topic ngat admin sana bweletse* *9๐onse omangokhala ndwiiiii muno osama commenta zanzake zakolopedwa* *10๐Muno zandale sitilola komaso kutumiza khani za sing'anga muno ayi๐ซ๐ซ๐ซ* *๐ฃ๐ฃndakusokosela mkulinga utamva tsatiran mallamulo kuti tiyendele limozi* *`๐ค๐ค MUMODZI MULI PHAMVU BY PANGOLINI` ๐ฆ๐ฆ๐ฆ๐ฅ๐ฅ๐ฅ*
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
TAKULNDILANU MUNON NDIPO KHALANI OMASUKA๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฝ๐ฝ
Takulandilani alendo anthu ku group lamacheza Atsikana ndi Anyamata Malamulo ali motele angati walowa kumene akuyenela kutumiza picture ndi kudzfotokozelaso muli 2 muno link ya group lina sitimalola kupatula lanthuli 3 osasankhana osankhana machezedwe muno nkazi kapena mamuna ali ndi ufulu kucheza amene akufuna muno 4 muno ma video olaula sakuloฤบdwa ukatumiza remove 5 osamulowela munthu inbox yake asadavomele kuti mupite ukapezeka ndi remove 6 Sunday ndi pic day aliyese amaponya pic osatumizayo tsiku limenelo amatulutsidwa 7 muno kungonkhala osamayankhula kapena osakometa remove 8 nkhani ya topic aliyese atha kulemba topic koma osalemba topic wina ataponya kale chonde ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ 9 chonde ngati mwawona kuti wina sadakuchezeleni bwino pezani admin akuthandizeni 10 muno nkhani zaku inbox zisafike pano pa group zithele konko 11 osatumiza ma sticker please ma sticker ena amankhala wonyoza nde osaponya please 12 mayina awa muno osatchula munthu ngati hule, fiti,kapolo ndi ena 13 osanyoza chipembedzo chazako muno ukapezeka remove Zikomo kwambili achibale nose muno ngati likumveka group chifukwa cha inuyo tiyeni tidzicheza Kutsatira Malamulo kut masiku ako opedzeka pano achuluke๐ฅฐ๐โฃ๏ธ๐๐๐
*WELCOME TO PHWETE LOSATHA GROUP* ๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐ *_MALAMULO ALI MOTELE MUNO_* (1๏ธโฃ) *Aliyese mulendo akalowa muno akuyenela kuponya picture yake komaso dzina ndikumudzi kwanu* (2๏ธโฃ) *Sitilola kuponya links ya group ina muno ukapezeka remove๐ฎโ* (3๏ธโฃ) *Sitilola zinthuzi zolawuula kapena ma video olawula ukapezeka removeโ๐ฎ* (4๏ธโฃ) *Sitilola kuponya sticker muno ukapezeka remove โ๐ฎ* (5๏ธโฃ) *Ma voice muno sitilola komas muno simopangila business ukapezeka remove*โ๐ฎ (6๏ธโฃ) *Aliyese osatengapo mbali muno after week mudzienda chikolopa kuyambila (25 message in 22 message out)* (7๏ธโฃ) *Osalowa ku inbox popanda chilolezo cha mwini wakeyo, akakupatsa chilolezocho za kuinbox zinthele konko zisafike pa group* (8๏ธโฃ) *Kupeza wachikondi nkololedwa ngati mwakondana pitilizani pokwanilitsa maloto Anu* (9๏ธโฃ) *Ngati muli ndi wachikondi wanu pa group chezani ndi wina aliyense koma mosapyola malire kupewa phokoso ndi okondedwa anuwo* (๐) *ngt ndiwe wa nsanje modzi pa uwu wiri wanu akuyanera kutuluka or ayi nonse limodzi* *_Chenjezo_*: _ngati Zachikondi zanu zikubweletsa chisokonezo pa group pano nonse mudzachotsedwa posayang'anira kuti ndindani eve admin_ *Ma program anthu ali motele muno* ๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐ (1๏ธโฃ) *Monday timakhala ndi topic 8:00pm* (2๏ธโฃ) *Tuesday timakhala ndi topic 8:00pm* (3๏ธโฃ) *Wednesday program ya Miyambi yomwe aliyense amayenera kutenga po gawo 8:00pm* (4๏ธโฃ) *Thursday timakhala ndi topic 8:00pm* (5๏ธโฃ) *Friday timakhala ndi topic 8:00pm* (6๏ธโฃ) *Saturday program ya tikudziweni yomwe tidzikhala tikucheza ndi mulendo 8:00pm* (7๏ธโฃ) *Sunday lililonse program ya tidziwane amai ndi abambo yomwe idzikhala pic day (ndiwe okwatila kapena uli single) kwa tsiku lonse* *_tiyeni tilemekezane wina ndi zake tisanyozane๐๐๐_* *Tisanyozelane zipembezo muno* *_Tiyeni malamulo tiwagwilitse tchito kuti Masiku onkhala nafe muno achuluke zikomo_* *Ndiudindo waliyese kutenga nao gawo muno* *_Done_by_administration_panel.com_*......๐๐๐คณ