Search the WhatsAd index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
Sharing of information regarding Global affairs pertaining to the End times(Akhiru Zaman)
Sharing of information regarding Global affairs pertaining to the End times(Akhiru Zaman)
*MALAMULO ATHU MUNO MU BULLETS MANOMA SILVER ๐ฅ ZAMASEWERO* โฝโฝโฝ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena ndi ma sticks ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* mphavu nyerere ๐๐๐๐๐ญ๐ณ๐ญ๐ณ๐ญ๐ณ๐ญ๐ณ mphavu bullets ๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น mphave silver ๐ฆ๐ท๐ฆ๐ท๐ฆ๐ท๐ฆ๐ท *umodzi pa machedza* ๐คธโโ๐คธโโ๐คธโโ๐คธโโ๐คธโโ