TAKULANDILANI ALENDO NONSE PANO PA KUPEZA WACHIKONDI WENIWENI 💞💞🥰 1)Mukalowa kumene ponyan Pic mkunena komwe mumakhala 💕 2) Osanyozana❌ 3)Osasankhana mitundu❌ 4)Osatumiza VN❌ 5) Osatumiza link yagulu lina❌ 6)Nkhan Zaku inbox osamabweletsa pagulu pano muzatulusidwa nonse❌ 8)Osaponya zolaula muno❌. 9) Sunday Pic day💕
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
MALAMULO:::::::::::::::::::::::::::::::::: (1) WOSAPONYA LINK YA GROUP LINA (2) ZANDALE KAPENA ZACHIPEMPHEZO NDI KUNYOZANA MUNO AYI ZIMENEZO AWA NDIMACHEZA TIYENI TIKONDANE WINA NDIZAKE (3) WOSATUMIZA CHINTHU CHOKHUZA ZOLAULA MUNO (4) WOSAYIMBA VOICE CALL PA GROUP (5) NGATI MUKUCHEZA NDI ZANU PANKHANI ZA MPIRA CHEZANI BWINOBWINO POSADUMPHA MALILE A ULEMU (6) SUNDAY TIMAKHALA NDI PIC DAY NDICHOLINGA CHOTI TIZIWANE (7) ZIWANI KUTI NDIUDINDO WAWINA ALIYESE KUTUMIZA ZINTHU ZOKHUZA MASEWELO A MPIRA KUTI GROUPLI LIBHEBHE ZIKOMO MAKOMA NONSE MASAPOTA A MA TEAM WOSIYANASIYANA✏️
𝕋𝕀ℙ𝔼ℤ𝔼 𝕄𝔸𝕃𝕀ℕ𝕂 𝕄𝕌ℕ𝕆 Welcome alendo nonse takulandilani khalani omasuka 🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️muno timalola kuponya malink ndi macheza basi🤺🤺🤺🤺🤺🤺🤺🤺🤺🤺Zosaloledwa muno ndi izi👇🏻👇🏻 𝗭𝗮𝘀𝗶𝗻𝗴'𝗮𝗻𝗴𝗮 𝗭𝗮𝗺𝗮𝗹𝗼𝗻𝗱𝗮 𝗞𝘂𝗽𝗼𝗻𝘆𝗮 𝗹𝗶𝗻𝗸 𝘆𝗼𝗺𝘄𝗲 𝘆𝗼𝗺𝘄𝗲𝘆𝗼 𝗸𝗼𝗺𝗮 𝗺𝗼𝗯𝘄𝗲𝗿𝗲𝘇𝗮 𝗯𝘄𝗲𝗿𝗲𝘇𝗮 ✖️✖️✖️✖️✖️Anzathu onyozera ma 𝗿𝗲𝗺𝗼𝘃𝗲 🙏🏻🙏🏻🙏🏻🙏🏻🙏🏻
*TAKULANDIRANI KU TIPEZE WACHIKONDI 💓💓* *MALAMURO NDI AWA* 👇 *1️⃣ALIYENSE AKUYENERA KUTENGA NAWO MBALI KUTI MACHEZA AKOME KOMASO KUTI TIPEZE WACHIKONDI MOSAVUTA👩❤️💋👨👨❤️👨* *2️⃣MULENDO UKAFIKA AKUYENERA KUPONYA PIC NDI KUNENA KOMWE UMAKHALA💃🕺* 🤳 *3️⃣MA LINK AMA GROUP ENA MUNO AI 👺👺* 4️⃣ *MA PROGRAM ATHU ALI MOTERE:* *MONDAY, WEDNESDAY NDI FRIDAY TIMAKHALA NDI* *TOPIC. NDIPO SUNDAY NDI PIC DAY* 💃🕺🤳 *5️⃣NKHANI ZA KU INBOX ZIZITHERO KUMWEKO* 🫐🫐🫐🫐🫐 *6️⃣KUCHEZERANA KUZIWANA KUMAONONGA GROUP KUMACHEZA NDI ALIYENSE* 🤺 *7️⃣VOICE NOTE MUNO AI & WEEK ILIYONSE TIMACHOSA ANTHU OSATENGA NAWO MBALI* 🤺🏹 *🌹🌹🌹TIPEZE WACHIKONDI*
TAKULANDILAN ALENDO MUNO PEZANI WACHIKNDl WANU Lemekezani malamulo 👇👇 1 Ukalowa ponya PIC ndikomwe umakhala 2 Ukafuna kucheza ndimkazi ku inbox uza ky admin 3 Osaponya ma Link a group yina ❌ 4 Audio or VN Ayi 5 muno ukapezeka ukulemba English ❌ 6 Ndiufulu waliyese kuponya mapono 7 Ngat sukutengapo mbali pa nkhani zose ❌ 8 Ngat ndi Stick yapono utha kuponya 9 Tsiku laTopic ndi limodz lachiwir madzulo kuyamba 7 o'clock 10 Tikhale okondana kuti group la2 lipite patsogolo 11 Oyambitsa voice chat join limove ❌ Lemekezan malamulo kuti masiku amuno achuluke
MALAMULO AGROUP INO NDI AWA✍️✍️👇👇👇 TIPEZE MALINK PANO 💯% 1 osatumiza ma video olaula kapena photo zolaura ukapezeka remove❌ 2 osatumiza zotsatsa malonda ukapezeka remove❌ 3 osatumiza ma stick ukapezeka remove❌ 4 Osatumiza zachipani ukapezeka remove❌ 5 Osatumiza ma vn kapena record ukapezeka remove❌ 6 tisasakhane mitundu ukapezeka remove❌ Kuponya malink ndi udindo wawina aliyese tiyeni tigawane ma link amene zathu wapepha zikomo Komaso kucheza ndikofunika Tiyeni ticheze Ma member nonse mukhare omasuka pamene mwalowa muno maramulo ndi amenewo tiyeni titsate malamuro kuti masiku okhara muno achuluke mwakoma nose munali ndine m'bale wanu mr Joseph admin anu baye ❤️🇲🇼🇲🇼
Mwalandilidwa. mabwana nose muno sitimaponya mafilimu. Mwaka thithi ndimaponya. Ma post amafilimu omwe atuluka or omwe atatuluse. Pali group limene ndimaponya mafilim. koma ndimayika. Okhao alipila timalipisa pa week kapena pa mwedzi mutha kutumiza ka dora ku number iyi 0998778946 Tilankhulen mukafuna kafuna kuziwa zambili tilakhule pa 📲 0983372539 osawopa