Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
Malo oyenera kwa iwo ali ndi njala ya Mulungu
MWISHO UMEKARIBIYA UNABII UNATIMIYA TUBU da Matayo 24.1
[link hidden — subscribe to view]
Cholinga Cha group ndikukambirana nkhani zokhuza dela lathu lamakanjiri kundale zadela ,chitukuko komanso mavuto amdela MALAMULO A GROUP (1) osatumiza zithunzi kapena ma kanema olawula (2) osatumiza ma link ama group ena pamudzi pano (3) osatukwanizana pa group pano (4) kulemekeza maganizo anzathu ,sitingaganize mofanana (5) osatenga nkhani zokambidwa pano mwachisawawa chifukwa anthu akhala ndimaufula olankhula zakukhosi kwawo mosaopa (6) obwela ndichisokonezo sasowa ndipo sitizachedwa kum'panga remove (7) munthu Ali ndiufulu olemba kapena kugwiritsa ntchito mawu ake pogawana uthenga (8) osatumiza nkhani zabodza zopanda umboni pa group Kupezeka ophwanya malamulo adzachotsedwa pa group (9) Group la friends of makanjira liziyamikira kapena kudzudzula andale ,akapezeka munthu obweletsao chisokonezo pa group posafuna anthu kuti adzudzule kapena kuyamikira andale ,munthuyo adzachotsedwa pa group car h
.