ZILIPATI,KWAGWANJI &ZAKUNDENDE, FRANCO PRODUCTION
MALAMULO ZILIPATI & ALIDELE & ZAKUNDENDE
1. Musaponye link ya gulu lina ukapezeka uzatulusidwa pomwepo.
2.Mulendo akalowa akuyenela kuponya pic ndikuzifotokoza komwe amachokela.
3.Sitilola mavideo olaula muno ukapezeka 🗻🗻 pomwepo.
4.Tisasalane mitundu kmaso zipembezo ai tonse ndi amodzi.
5.Ma stiker omwe timalola ndi awa😍🥰✋🤔☝️🤣 kma ena aja saloledwa ai.
6.Mukalowelana ku inbox zithele komweko basi.
7. Ndi udindo wa wina aliyese kuponya nkhani osasiyila ma admin okha a
8. Osaponya voice record muno kmaso osamangowelenga ngati muli mu library ai
9. Weekend timaponya mapic kuti tidzidziwana