Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
MALAMULO ZILIPATI & ALIDELE & ZAKUNDENDE 1. Musaponye link ya gulu lina ukapezeka uzatulusidwa pomwepo. 2.Mulendo akalowa akuyenela kuponya pic ndikuzifotokoza komwe amachokela. 3.Sitilola mavideo olaula muno ukapezeka 🗻🗻 pomwepo. 4.Tisasalane mitundu kmaso zipembezo ai tonse ndi amodzi. 5.Ma stiker omwe timalola ndi awa😍🥰✋🤔☝️🤣 kma ena aja saloledwa ai. 6.Mukalowelana ku inbox zithele komweko basi. 7. Ndi udindo wa wina aliyese kuponya nkhani osasiyila ma admin okha a 8. Osaponya voice record muno kmaso osamangowelenga ngati muli mu library ai 9. Weekend timaponya mapic kuti tidzidziwana
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
🇿🇦🇲🇼🇿🇦🇲🇼🇿🇦🇲🇼🇿🇦🇲🇼🇿🇦🇲🇼🇿🇦
0
Gululi ndilaulele. Nde pasapezeke utumiza zinthu zosagwikizana ndi gululi Nthawi yomweyo azachosedwa. Ndipo pakanyasa kwambiri timapempha seka. Only admin ndiamene akumakwanisa kutumizapo uthenga. Nde tikaliseka pasamapezeke wina okalupa as if ndilolipila. Zichepe zimenezo.