ΧΧ€Χ©Χ ΧΧΧΧ ΧΧ§Χ‘ Χ§ΧΧΧ¦ΧΧͺ ΧΧΧΧΧΧ‘ΧΧ€ Χ©Χ WhatsAd ΧΧΧ ΧΧΧ¦ΧΧ ΧΧͺ ΧΧΧΧΧΧͺ ΧΧΧΧͺΧ¨.
ΧͺΧΧ¦ΧΧ ΧΧΧͺ ΧΧΧΧ ΧΧ§Χ‘ ΧΧ§ΧΧΧ¦ΧΧͺ Χ©Χ WhatsAd
MWALANDILIDWA NONSE NDIPO KHALANI OMASUKA. ALENDO MUKANGOLOWA KUMENE PONYANI PIC NDIPO MUDZIFOTOKONZERE NOKHA KUTI NDINU NDANI NDIPO MUMAKHALA KUTI. NDIPO TSATILANI MALAMULO ONSE AMGULU LINO MUKATERO MUDZAKHALITSA. LEMEKEZANI MALAMULO AMGULU LINO NDIPO NAWO ADZAKULEMEKEZANI. GROUP CREATED BY ABDUL RASHID CHIKOPA.
Χ§ΧΧ©ΧΧ¨ ΧΧΧΧ Χ ΧΧΧΧΧͺ, Χ€Χ¨ΧΧ ΧΧΧ¨ΧΧ ΧΧΧ€Χ©Χ¨ΧΧΧΧͺ Χ€Χ¨Χ‘ΧΧ Χ-WhatsAd.
*MALAMULO ATHU MUNO MU BULLETS MANOMA SILVER π₯ ZAMASEWERO* β½β½β½ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena ndi ma sticks ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* mphavu nyerere ππππππ³ππ³ππ³ππ³ mphavu bullets π¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉ mphave silver π¦π·π¦π·π¦π·π¦π· *umodzi pa machedza* π€Έββπ€Έββπ€Έββπ€Έββπ€Έββ
Malamulo aa group ali mothelo 1 Vn yoletsedwa ββ 2 macheza katiti β β 3 Voice chat yoletsedwa ββ 4 kutukwanana muno ay ββ 5 Nkhani za mpira β β β 6 ma stick No ββ 7 mautenga okuza team ina ay ββ 8 ma link aa group lina ay β β 9 Lamulo lomaliza chonde mokumbepa all members monga masapoter aa team yathu ya NBB NYASA BIG BULLETS chonde osanyosa ma admin tikale okondana kulakwisa admin timausana kut tikotse mvuto limenelo zikomo maule notse πππππ