חפשו באינדקס קבוצות הוואטסאפ של WhatsAd כדי למצוא את הטובות ביותר.
תוצאה אחת באינדקס הקבוצות של WhatsAd
𝐍𝐘𝐀𝐒𝐀 𝐁𝐈𝐆 𝐁𝐔𝐋𝐋𝐄𝐓𝐒 𝖬𝖶𝖠𝖫𝖠𝖭𝖣𝖨𝖫𝖨𝖣𝖶𝖠 𝕄𝔸𝕃𝔸𝕄𝕌𝕃𝕆 𝔸𝕃𝕀𝕄𝕆𝕋𝔼𝕃 KUPEZEKA UTAPONYA LINK YOSIYANA NDI GROUP INO REMOVE ❌❌ KUNOKO NDIKWA MAULE NSITUKUFUNA NEBA UKAPEZEKA REMOVE ❌❌ KUPONYA DZOLAULA UKANGOPEZEKA REMOVE ❌❌ VN OR VOICE CHAT 👉 STICKERS NSITIMAGWILISA NTCHITO CHIFUKWA KUPEZE KWA BUNDLE NDKOSIYANA❌❌ KUCHEZA MOSASAKHANA MITUNDU KOMASO KOCHOKELA POTI TOSE NDIFEANA ABANJA LIMOZI🔥🔥🔥🔥🔥 ALIYESE ALINDIKUTHEKELA KOPONYA KHANI OR VIDEO KOM ZOKHUZA BULLETS OSAPONYA ZOSIYANA UKANGOTELE REMOVE ❌❌ KWAMEN AKUZIWA KUTI CHILIPO CHOLAKWIKA KOM MULIOMASUKA KUWAPEZA ADMIN NDIKUWAFOTOKOZELA KUTI MUZIYENDELABE LIMOZI GROUP THAWI IKAKWANA 09:30PM TIZILISEKA KUPANGILA AKAPASULE KUONONGA ASING'ANGA PEZANI GROUP YANU 👊👊🧰✂️✂️ 🙌🙌🙌🙌🙌📛📛📛❤️🔥❤️🔥❤️🔥 MAULE🔥🔥🔥 MOTO TINABWELA KUZAKHALA⚽⚽⚽⚽✅✅✅🤝🤝🤝
קישור הזמנה מאומת, פרטי חברים ואפשרויות פרסום ב-WhatsAd.
*MALAMULO ATHU MUNO MU BULLETS MANOMA SILVER 🥈 ZAMASEWERO* ⚽⚽⚽ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena ndi ma sticks ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* mphavu nyerere 🐜🐜🐜🐜🇭🇳🇭🇳🇭🇳🇭🇳 mphavu bullets 🇦🇹🇦🇹🇦🇹🇦🇹 mphave silver 🇦🇷🇦🇷🇦🇷🇦🇷 *umodzi pa machedza* 🤸♂🤸♂🤸♂🤸♂🤸♂
A COLLECTION OF SEVENTH DAY ADVENTIST CHURCH HYMNS