G.D NATURAL HERBS
*MWALANDILIDWA NONSE* ‼️
↪️ Pamudzi pano osaponya chilichonse kupatura kufunsa mafunso okhudza za umoyo komansotu ngati muli mu South Africa tili ndi ma herbs omwe timagulitsa ndipo timatumiza kulikonse muno mu South Africa and ma Herb athu ndiwovomelezeka ndi dziko la Sound Africa;
↪️ Komanso ngati mungafune kugura koma muli dziko lina monga Malawi ndekuti mutha kupeza means yanu ya transport mukapanga order fukwa njira zathu zitha kuchedwerapo, the following are some of the diseases that we deal with.
1. High kapena low blood pressure/nthenda iliyonse ya mtima.
2. Shuga (diabetes) ngakharenso mabara a shuga.
3. Kuthandiza mayi kutenga pakati kapena Bambo kupereka mimba.
4. Mphavu zochuluka za kuchipinda ndi kuletsa kuthila nsanga etc.
5. Nthenda ya gas mmimba komanso acidity ma herbs alipo.
6. Nthenda yamuchikhodzodzo, Urinary Tract lnfection.
7. Kuonjezera chitetezo m'thupi (immunity booster) for HlV + or -.
8. Kuchapa Nthupi ndi kuchotsa zoyipa zonse (Detoxification).
9. Zilonda za Nthupi kapena za mmimba zomwe ma Ulcers.
10. Ziphuphu, Masara/Zikanga ndingoti nthenda iliyonse yapakhungu.
11. Tilinso ndi ma herb a chifuwa chilichonse ngakhare cha Asthma.
12. Kuletsa kuphwanya kwa nsana, mchiwuno tingoti mma joint monse.
13. Nthenda zonse zopatsirana pogonana STls include HlV.
14. Ngati mmageya zonunkha kaya kudzimbidwa (Indigestion).
15. Tipamezekanso ndi ma herb othandiza kuchotsa nkhawa (stress and anxiety).
16. Ngati muli ndi vuto losowa tulo (Insomnia) ndiyankhureni.
17. Komanso ena muli ndi vuto loyiwalayiwala (memory loss) ndiyankhureni.
18. Ena muli ndi dzimfine dza mgonagona musavutike ndiyankhureni.
19. Ngati mmatulutsa period yambiri kapena simupangiratu ndiyankhureni.
20. Nthenda iliyonse ya liver, kidney, and ma lungs ma herb ake alipo.
21. Nthenda ya hemorrhoids (Likango) ma herb akenso alip sure.
22. Kaya muli ndi zotupa za mchiberekero kaya cervical cancer ndiyankhureni.
23. Kaya muli ndi Mauka, fungus, in short ndingoti matenda onse omwe muli nawowo ndiyankhureni basi.