MIGHTY WANDERERS SUPPORTERS 🇲🇼
*WELCOME TO MIGHTY WANDERERS SPORTS GROUP*🐜🐜🐜🐜
Awa ndi malamulo apa group pano uyenela kusatila👇
1, takulandilani alendo nose khalani omasuka
2 ma stick muno sitilola❌
3, ma voice osakhala ampira sitilola❌
4,ma video osakhala ampira sitilola❌
5,ma links a group Ina sitilola❌
6, osanyonzana zipemphenzo muno❌
7, nkhani zaku in box kwanu osazibwelenza muno
8, osatukwanana muno mzako ngt walakwinza malankhulidwe lankhuleni mwaulemu
9, nkhani za ndale sitilola❌
10,group lino ndila noma mukamuona munthu wa team ina muziwiseni admin azapanga remove pompo pompo
11, muno sitimafusila zibwez ngt munthu wakusangalasani pitilen ku in box kwake ost pa group pano ok
12, munthu ukangokhala 3 days committe oro update iliyonse ulibe usapangidwa remove
13, ndi udindo wa aliyense kutenga nawo gawo pa group pano osamango wasiila admin okha Ai
14, timakamba za team yathu 90% zama team ena Malawi muno 5% ma team akunja 5%
*KHALANI OMASUKA ARENDO NOSE*🙏
*LIVE UPDATES FROM LALI LUBAN*🇲🇼🐜🐜🐜🐜🐜🐜🐜