NBB🚩🚩🚩🇦🇹🇦🇹 NOMA🇪🇺🇪🇺🇬🇷🇬🇷 SILVER🇧🇼🇧🇼🇧🇼
NBB🇦🇹🇦🇹NOMA🇪🇺🇪🇺SILVER STRIKERS🇧🇼🇧🇼
Takulandilan ku group la masapota ampira okonda ma team awo mwamtendere.
Muno timalimbikisa kukondana wina ndi mzake osat mikangano koma macheza okhuza mpira bas. Ochilimika kuponya nkhan pazikhakala mwayi wa mphoto ya ma bundle a internet
*Malamulo agroup lino*
Zolesedwa
1.osaponya link la group Lina ❌❌❌❌ukatero remove
2.osaponya chilichonse choonesa kulaula❌❌❌❌ukatero remove
3.osachula maina oyambisa mikangano muno monga:kapado/nkhumba fc,chingambwe fc,nyau fc❌❌❌❌ ukapezeka remove.
4.osaponya ma sticker,voice note,kutukwana❌❌❌❌Ukapezeka remove
5.siku la mpira(match day)ndi siku longoponya ma updade osasakaniza nkhan kupereka mpata kwa mamembala kusatira mpira.
6.kupereka update yabodza❌❌❌❌
Ukapezeka remove
7.kusakhala active kwa 2weeks❌❌❌❌remove
8.Ili ndi group la za mpira only osatumiza zosemphana ndi mpira monga za ndale,nkhan osat zampira❌❌❌❌ukapezeka remove
9.ukalowa pa chat kukakhala game tiziyesesa kusatila mamessage omwe atizidwa kale kut tione mmene ma results mmene akuyendera kupewa mafunso ot game ikuyenda bwanji,wagolesa ndan,zikutha bwanji,izi zimapwetekesa omwe amuluza.
11.oyambisa chisokonezo muno❌❌❌❌remove
*Kutumiza nkhan ndi kwa aliyense osadikilira ma admin okha*
Ngat mwawona vuto pa malamulowa pezanani ndi admin ndipo tulani nkhawa zanu.
Masiku ena tizikhala ndi mway ocheza ndi alendo koma a mpira okhaokha.
*Maule,manoma ndi ma bankers 🚩🚩🚩🇦🇹🇦🇹🇬🇷🇬🇷🇬🇷🇪🇺🇪🇺🇪🇺🇧🇼🇧🇼🇧🇼🇧🇼pamodz imapanga flames🇲🇼*
Zikomo khalan omasuka
*By adminstration*