𝐈𝐒𝐋𝐀𝐌𝐈𝐂 𝐁𝐎𝐎𝐊𝐒,𝐀𝐏𝐏𝐒,𝐏𝐃𝐅&𝐋𝐈𝐍𝐊𝐒🌍
*Malamulo apamudzi pano nawa👇🏽*
```(1)Gululi ndilachisilamu,motero ngati mumadana ndi chisilamu kuli bwino kungofumuka mwaulemu kusiyana nkuti🤺🤺🤺```
```(2)Cholinga cha gululi nchoti tizitha kugawana zinthu monga:```
_➡Islamic Documents_
_➡Islamic Links_
_➡Applications(APK)_
```Kuonjezera apo timathanso kuthandizana ma settings a phone kuphatikizapo,whatsapp,Facebook,Twitter,Instalgram...```
```(3)Simuli oloredwa kutumiza zinthu izi:```
~➡Videos📺~
~➡Audios🎶~
~➡Voices🎤~
~➡Pictures🏝~
~➡Ulariki💂muno ayi~
```(4)Ziyankhulo zamuno ndizinai zokha(Arabic,English,chichewa ndichiyao zinazo sizikulolodwa.```
```(5)Osapanga tag group lino kustatus kwanu muzachotsedwa limodzi ndistatus yanuyo.```
*⚠️Munthu akatumiza zoipa immediately achotsedwa limodzi ndi opanga tag.*
*MONI WAMUNO NDIKUPEREKA SALAAM.*