CommunitiesBIG BULLETS SUPPORTERS โšฝ๐Ÿ’ƒ๐Ÿ•บ๐Ÿƒโ€โ™‚๏ธ

BIG BULLETS SUPPORTERS โšฝ๐Ÿ’ƒ๐Ÿ•บ๐Ÿƒโ€โ™‚๏ธ

200+ membersFrench

About this community

MWALANDILIDWA NONSE NDIPO KHALANI OMASUKA. ALENDO MUKANGOLOWA KUMENE PONYANI PIC NDIPO MUDZIFOTOKONZERE NOKHA KUTI NDINU NDANI NDIPO MUMAKHALA KUTI. NDIPO TSATILANI MALAMULO ONSE AMGULU LINO MUKATERO MUDZAKHALITSA. LEMEKEZANI MALAMULO AMGULU LINO NDIPO NAWO ADZAKULEMEKEZANI. GROUP CREATED BY ABDUL RASHID CHIKOPA.

French
Unlock / View Community

Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.

Related communities

BULLETS โ™‰ MANOMA ๐Ÿ’™ SILVER ๐Ÿฅˆ ZAMASEWERO

*MALAMULO ATHU MUNO MU BULLETS MANOMA SILVER ๐Ÿฅˆ ZAMASEWERO* โšฝโšฝโšฝ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena ndi ma sticks ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* mphavu nyerere ๐Ÿœ๐Ÿœ๐Ÿœ๐Ÿœ๐Ÿ‡ญ๐Ÿ‡ณ๐Ÿ‡ญ๐Ÿ‡ณ๐Ÿ‡ญ๐Ÿ‡ณ๐Ÿ‡ญ๐Ÿ‡ณ mphavu bullets ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น mphave silver ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡ท๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡ท๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡ท๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡ท *umodzi pa machedza* ๐Ÿคธโ€โ™‚๐Ÿคธโ€โ™‚๐Ÿคธโ€โ™‚๐Ÿคธโ€โ™‚๐Ÿคธโ€โ™‚

900+ membersBUG

๐Ÿ”ฅโšฝ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ NBB VS NOMA $ SILVER SUPPORTERS GROUP ( A)๐Ÿ”ฅโšฝ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ

MALAMULO ATHU ALI MOTERE PA GROUP PANO๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿฅณ๐Ÿฅณ๐Ÿฅณ๐Ÿฅณ๐Ÿฅณ๐Ÿฅณ๐Ÿซ ๐Ÿซ ๐Ÿฅณ (1)Sitilora kutumiza ma links ena Muno ukapezeka remove ๐Ÿ˜ก๐Ÿ˜ก (2)Muno kutumiza nkhani za spots 90% macheza 10% (3)Ndi udindo WA aliyense kutumiza sports osadikira adimin okha okha komanso wa (0 )comment azapangidwa remove (4)Muno ma vn, ma porno,zandale ,zachipembedzo ,ma stickers,timaletsa only sports bas (5)Za ku inbox zithere komko zisafike pa group pano yemwe azapezeke remove (6)

900+ membersSWE

๐Ÿ…ฑ๏ธFCB NYASA BIG BULLETS SPORTS UPDATES ๐Ÿ”žโšฝ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ž

WELCOME TO FCB NYASA BIG 2๏ธโƒฃ0๏ธโƒฃ2๏ธโƒฃ5๏ธโƒฃ SUPPORTERS GROUP NDIPO MALAMULO ATHU ALI MOTEREโฌ‡๏ธโฌ‡๏ธโฌ‡๏ธ 1๏ธโƒฃ TIKONDANE WINA NDI MZAKE TOSE NDIFE BANJA LIMODZI MONGA MAPALE 2๏ธโƒฃOSAMASANKHANA MITINDU KAPENA CHIPEMBEZO 3๏ธโƒฃ NDI UDINDO WA WINA ALIYETSE KUTUMIDZA UPDATE PA GROUP PANO 4๏ธโƒฃ NO PORNO VIDEO OR PHOTO( ZITHUZ KAPENA MA VIDEO OLAURA MUNO AYI NDI ZOLETSEDWA 5๏ธโƒฃ OSAMAPONYA LINK YA GROUP LINA MUNO 6๏ธโƒฃ OSAMAPONYA MA STICKER MUNO 7๏ธโƒฃ NO VN MUNO POKHA POKHA ITAKHALA SPORTS 8๏ธโƒฃ WINA ALIYETSE AZITENGA MBALI MKAKHALA 1 WEEEK OSATENGA MBALI MZATULUSIDWA 9๏ธโƒฃ OSAMANYOZANA ๐Ÿ”Ÿ NKHAN ZA PA GROUP PANO ZIZIKHALA 90% ZA MPIRA MBALI INAYO TIKHOZA KUMACHEZALO DZINA 1๏ธโƒฃ1๏ธโƒฃ ZA NDALE MUNO AYI UKAPEZEKA REMOVE 1๏ธโƒฃ2๏ธโƒฃ NKHAN ZA GROUP PANO ZIZITHERA POMPANO NOT KU INBOX 1๏ธโƒฃ3๏ธโƒฃ MKAPEZA VUTO PITANI KU INBOX KWA ADMIN NDIPO TSATILAN MALAMULO ZIKOMO *BY ADMIN MUNSA ENTERTAINMENT ๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™

900+ membersLUG

๐ŸŽช๐Ÿฟโœ…๐Ÿ…ฑ๏ธNYASA BIG๐Ÿšฉ โœ… BULLETS๐Ÿ“…โ™ฅ๏ธ๐Ÿ“… FCS ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ…ฑ๏ธSPORTS ONLINE MR JMS โœ…โ€ผ๏ธ๐Ÿ…ฑ๏ธ๐Ÿ’ฅโ‰๏ธ

*WELCOME TO ๐Ÿ…ฑ๏ธ๐Ÿ…ฑ๏ธ๐Ÿฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น FCB NYASA BIG BULLETS* *MALAMULO ATHU ALI MOTELE*๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡ 1๏ธโƒฃ๐Ÿฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น *Tiyeni tikondane ngat banja limodzi* 2๏ธโƒฃ๐Ÿฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น *Muno kunyozana ayi ๐Ÿคชngat wina wapezeka akunyonza anzake remove ๐ŸšฎโŒ๐ŸŒ๏ธ* 3๏ธโƒฃ๐Ÿฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น *Kuponya nkhani za masewelo si ntchito ya admin okha ayi ๐Ÿค“kma aliyese* 4๏ธโƒฃ๐Ÿฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น *Za masewelo za kunja ngakhalenso kuno kwathu ndye zofunika koma zikhale zoona* 5๏ธโƒฃ๐Ÿฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น *Ngati mwalowelana ku inbox zithere komweko muno ayi* (koma osalowelana opanda chilorenzo ayi) 6๏ธโƒฃ๐Ÿฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น *Muno osaponya ma links agroup ina,Ukapezeka remove ๐ŸšฎโŒ๐ŸŒ๏ธ* (sitilola maliki agrp ina) 7๏ธโƒฃ๐Ÿฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น *Muno aliyese osatenga mbali timamutulusa cox muno simongokhala chete ayi* (plus group ili sila asing'anga ai koma la mpira) 8๏ธโƒฃ๐Ÿฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น *No VN, Porn videos, Stickers and ma photo alaula!* *Muno zonse tantchulazi sitilola Ukapezeka remove ๐ŸšฎโŒ*๐Ÿšญ 9๏ธโƒฃ๐Ÿฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น *Zandale muno ayi, za chipembezo munso ayi, kutukwana ayinso๐Ÿค“ ukapeza remove ๐ŸšฎโŒ๐ŸŒ๏ธ* ๐Ÿ”Ÿ๐Ÿฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น *Muno 95% ndi nkhani za bullets bas 5% osalayo ya ma team ena* 1๏ธโƒฃ1๏ธโƒฃ๐Ÿฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น *Kupanga left muno ndye kuti zampira simbali yako* 1๏ธโƒฃ2๏ธโƒฃ๐Ÿฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น *KUTSOGONZA MULUNGU NDYE CHINTHU CHOPAMBANA KWABASI* 1๏ธโƒฃ3๏ธโƒฃ๐Ÿฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น *GULU LIZINKHALA LOSEKA KUYAMBIRA 10:30pm FOR SECURITY REASONS MALINGA NDI ANZATHU OFUNA KUTUMIZA ZOSAYENERA* *๐Ÿ“ฐ๐Ÿ“By your Administration* *Ngati mwalikonda group ili, tsatilan malamulo onsewa kuti tikhale limodzi bye bye for now* Don't forget (We are here for the football) *FOREVER MAULE ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น๐Ÿฟ๐Ÿฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ*

600+ membersTurkish

NYASA BIG BULLETS FC 2025/26

Malamulo aa group ali mothelo 1 Vn yoletsedwa โŒโŒ 2 macheza katiti โœ…โœ… 3 Voice chat yoletsedwa โŒโŒ 4 kutukwanana muno ay โŒโŒ 5 Nkhani za mpira โœ…โœ…โœ… 6 ma stick No โŒโŒ 7 mautenga okuza team ina ay โŒโŒ 8 ma link aa group lina ay โŒ โŒ 9 Lamulo lomaliza chonde mokumbepa all members monga masapoter aa team yathu ya NBB NYASA BIG BULLETS chonde osanyosa ma admin tikale okondana kulakwisa admin timausana kut tikotse mvuto limenelo zikomo maule notse ๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™

600+ membersNYA

AGAINST SUPPORTERS UNIONโšฝโšฝ

*_Yแดแดœส€ สŸแดsแด‡ แดแดœส€ แด˜ส€ษชแดส€ษชแด›ส๐Ÿ˜€๐Ÿ‘_* *_RULES FOR AGAINST SUPPORTERS UNION_* 1๏ธโƒฃEnglish only please and We are not English teachers learn to accomodate people of different languages as they try to discuss in English 2๏ธโƒฃNo promotion of links (group/spam). 3๏ธโƒฃOnly footballers pictures are allowed 4๏ธโƒฃMake sure u are part of the group conversations. 5๏ธโƒฃFeel free to troll clubs. 6๏ธโƒฃFeel free to post football updates. 7๏ธโƒฃNo Political TalksโŒ 8๏ธโƒฃDon't abuse any group member. 9๏ธโƒฃ Posts must be in tandem with football 1๏ธโƒฃ0๏ธโƒฃRepeat and chronic offenders will be banned permanently 1๏ธโƒฃ2๏ธโƒฃRespect all members and admins regardless of age, gender, race, nationality and tribe 1๏ธโƒฃ3๏ธโƒฃNo nude pictures and porn videos allowed. posting porn stuff in the group will lead to immediate removal 1๏ธโƒฃ4๏ธโƒฃPlease do not discuss any religious matters or political parties in the group 1๏ธโƒฃ5๏ธโƒฃAddress your fellow members and admins with respect *NOTE:* *WE SET RULES FOR A PURPOSE IF U CANT FOLLOW OUR RULES DONT JOIN US*

600+ membersEnglish