Communities🏆🇦🇹FCB🇬🇺CHTPA 🇮🇱NOMA🇸🇨B.E 🇸🇲& 🇳🇫MOYALE &🇪🇬 CIVO🏆🥇

🏆🇦🇹FCB🇬🇺CHTPA 🇮🇱NOMA🇸🇨B.E 🇸🇲& 🇳🇫MOYALE &🇪🇬 CIVO🏆🥇

900+ membersSSW

About this community

🏆🥈🇦🇹🇪🇺🇧🇼🇮🇴🇵🇫🇬🇱🏆🥇 *MALAMAULO ATHU ALI MOTELE.👇🏻* 🇦🇹 *BULLETS* 🇪🇺 *MANOMA* 🇦🇷 *SILV* 🇬🇷 *BLUE E.* *(( ADMIN WANKULU 👉🏼* *CHANCY HYC* *CHIMA ))* 👨‍💻🥈 🇦🇹 *MADIMIN ENA ALI MOTELE _MARTIN_ GIFT & NELSON* 👨‍🎨 ⚽ *Sports* Aliyense Atha Kutumiza always 📻📻🇲🇼 🇪🇺 ```Sapota Ukalowa Tumizani Picture Yako ndi Team Yako. 🇦🇷Kunyozana Kapena Kutukwana Muno Ayi❌ 🇦🇿Tiyeni Tisapote Ma Team athu Monga ndife Amòdzi 🇬🇷Aliyese Azichedza Ndi Nzake Kupewa 👉🏻Remove 🇦🇹Tikakupeza kuti Sukucheza 2 Weeks Yonse👉🏻 Remove 🇪🇺Za ku inbox Zithele Komweko Masapota 🇦🇿Nthawi Ya Game aliyeee Atha kutumiza Zotsatira 🇦🇷Vn Muno ayi ❌ 🇬🇷Nyimbo Tumizani any Song. Bola osapyola muyeso English muno ayi mlibe azungu 🇲🇼 ❌ Zandale ayi ukapedzeka ndi remove 🇲🇭❌ Ngat ukubwela ndichisokonedzo remove ❌🇲🇼 NGAT PALI VUTO PENA OR SIMUNAVETSE FUSANI MA ADIMIN ALIPO KUT ATITHANDIZE 🛡️🇲🇼 🇸🇽NO MA VIDEO OLAULA MUNO MA PORNO AI ❌ ® Martin@ ma adimin wotse tigwile ntchito molimbika pamozi ndima members athu 🇲🇼 Sports parliament, ZBS sports, times sports bembeke sports,⚽🏐🛡️🇲🇼🔥🔥ndingot mwakoma notse buy buy 🙏

SportsAISSW
Unlock / View Community

Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.

Related communities

BULLETS ♉ MANOMA 💙 SILVER 🥈 ZAMASEWERO

*MALAMULO ATHU MUNO MU BULLETS MANOMA SILVER 🥈 ZAMASEWERO* ⚽⚽⚽ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena ndi ma sticks ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* mphavu nyerere 🐜🐜🐜🐜🇭🇳🇭🇳🇭🇳🇭🇳 mphavu bullets 🇦🇹🇦🇹🇦🇹🇦🇹 mphave silver 🇦🇷🇦🇷🇦🇷🇦🇷 *umodzi pa machedza* 🤸‍♂🤸‍♂🤸‍♂🤸‍♂🤸‍♂

900+ membersBUG

🔥⚽🇲🇼 NBB VS NOMA $ SILVER SUPPORTERS GROUP ( A)🔥⚽🔥🇲🇼🔥🇿🇦

MALAMULO ATHU ALI MOTERE PA GROUP PANO🔥🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🥳🥳🥳🥳🥳🥳🫠🫠🥳 (1)Sitilora kutumiza ma links ena Muno ukapezeka remove 😡😡 (2)Muno kutumiza nkhani za spots 90% macheza 10% (3)Ndi udindo WA aliyense kutumiza sports osadikira adimin okha okha komanso wa (0 )comment azapangidwa remove (4)Muno ma vn, ma porno,zandale ,zachipembedzo ,ma stickers,timaletsa only sports bas (5)Za ku inbox zithere komko zisafike pa group pano yemwe azapezeke remove (6)

900+ membersSWE

NBB🚩🚩🚩🇦🇹🇦🇹 NOMA🇪🇺🇪🇺🇬🇷🇬🇷 SILVER🇧🇼🇧🇼🇧🇼

NBB🇦🇹🇦🇹NOMA🇪🇺🇪🇺SILVER STRIKERS🇧🇼🇧🇼 Takulandilan ku group la masapota ampira okonda ma team awo mwamtendere. Muno timalimbikisa kukondana wina ndi mzake osat mikangano koma macheza okhuza mpira bas. Ochilimika kuponya nkhan pazikhakala mwayi wa mphoto ya ma bundle a internet *Malamulo agroup lino* Zolesedwa 1.osaponya link la group Lina ❌❌❌❌ukatero remove 2.osaponya chilichonse choonesa kulaula❌❌❌❌ukatero remove 3.osachula maina oyambisa mikangano muno monga:kapado/nkhumba fc,chingambwe fc,nyau fc❌❌❌❌ ukapezeka remove. 4.osaponya ma sticker,voice note,kutukwana❌❌❌❌Ukapezeka remove 5.siku la mpira(match day)ndi siku longoponya ma updade osasakaniza nkhan kupereka mpata kwa mamembala kusatira mpira. 6.kupereka update yabodza❌❌❌❌ Ukapezeka remove 7.kusakhala active kwa 2weeks❌❌❌❌remove 8.Ili ndi group la za mpira only osatumiza zosemphana ndi mpira monga za ndale,nkhan osat zampira❌❌❌❌ukapezeka remove 9.ukalowa pa chat kukakhala game tiziyesesa kusatila mamessage omwe atizidwa kale kut tione mmene ma results mmene akuyendera kupewa mafunso ot game ikuyenda bwanji,wagolesa ndan,zikutha bwanji,izi zimapwetekesa omwe amuluza. 11.oyambisa chisokonezo muno❌❌❌❌remove *Kutumiza nkhan ndi kwa aliyense osadikilira ma admin okha* Ngat mwawona vuto pa malamulowa pezanani ndi admin ndipo tulani nkhawa zanu. Masiku ena tizikhala ndi mway ocheza ndi alendo koma a mpira okhaokha. *Maule,manoma ndi ma bankers 🚩🚩🚩🇦🇹🇦🇹🇬🇷🇬🇷🇬🇷🇪🇺🇪🇺🇪🇺🇧🇼🇧🇼🇧🇼🇧🇼pamodz imapanga flames🇲🇼* Zikomo khalan omasuka *By adminstration*

600+ membersZUL

GB ISIAN 3ANOMALI #2

MINTA PERMINTAAN AJA DULU SEMUANYA NNTI DI ACC KO TANKS •━━━━━━•𖤌✠✯⋅ஜ۩۞۩ஜ⋅✯✠𖤌•━━━━━━━• 𝐖𝐀𝐋𝐂𝐎𝐌𝐄 𝐉𝐔𝐑𝐀𝐆𝐀𝐍 *ᴍᴀsᴜᴋ ᴀᴊᴀ ɢᴀᴜsᴀʜ ʀᴀɢᴜ ᴘʀᴏsᴇs ᴜʟᴀɴɢ‼️* * *ᴘᴇʀᴍɪɴᴛᴀᴀɴ ᴅᴜʟᴜ ᴀᴊᴀ ɴᴀɴᴛɪ ɢᴡ ᴀᴄᴄ ᴀᴅᴍɪɴ ʟᴀɢɪ sɪʙᴜᴋ* * *ɢʙ ʟᴀɢɪ ᴅɪ ᴘᴜsʜ ᴅɪ ʜᴀʀᴀᴘᴋᴀɴ ᴊᴀɴɢᴀɴ ᴘᴀᴅᴀ ᴏᴜᴛ ʏᴀᴋ* * *ʟᴜ ɴʏᴀʀɪ ᴛʀx ᴅɪᴍᴀɴᴀ? ᴋᴀʟᴀᴜ ᴅɪsɪɴɪ ᴡᴀᴊɪʙ ᴍᴄ sɪɴɪ‼️* ──────•-•────── •━━━━━[𝘼𝘿𝙈𝙄𝙉 𝙐𝙏𝘼𝙈𝘼]•━━━━━• *[link hidden — subscribe to view] [contact hidden] [SURZZZ]* 𝗦𝗘𝗟𝗔𝗜𝗡 𝗡𝗢𝗣𝗘 𝗗𝗜 𝗔𝗧𝗔𝗦 𝗖𝗟𝗢𝗡𝗘 !! *GA PENTING GAUSAH CHAT* *SPAM LEBIH 3X BLOKIR* ──────•-•────── *ALL INFO GB ISIAN 3ANOMALI* [link hidden — subscribe to view] ──────•-•────── *ALL PT OFFLINE* *[link hidden — subscribe to view] [contact hidden] [MBUL]* *[link hidden — subscribe to view] [contact hidden] [PENYUN]* *《ALL OWN BIASA BERIDENT》* *[link hidden — subscribe to view] [JUXXY]* *[link hidden — subscribe to view] [VADS]* *[link hidden — subscribe to view] *[link hidden — subscribe to view] *[link hidden — subscribe to view] *[link hidden — subscribe to view] *[link hidden — subscribe to view] *[link hidden — subscribe to view] *[link hidden — subscribe to view] OPEN OWN BIASA BAWA DANA 15 OPEN OWN SUNG CHAT KE NOPE SURZZZ ATASS * ──────•-•────── * *MC AN 30 KEATAS WAJIB KE ADMIN GRUP!!!!* *- sᴇʟᴀɪɴ ɴᴏᴍᴏʀ ᴅɪ ᴀᴛᴀs ᴄʟᴏɴᴇ / ʀɪᴘᴘᴇʀ* *- ᴋᴇᴛᴇᴍᴜ ᴏᴡɴ ʏᴀɴɢ ɴɢᴀᴋᴜ² ᴡᴀ ᴅɪ ᴅᴇsᴋʀɪᴘsɪ / ɴᴏᴘᴇɴʏᴀ 𝟸 ?ᴊᴀɴɢᴀɴ ᴅɪᴘᴇʀᴄᴀʏᴀ ɪᴛᴜ ᴄʟᴏɴᴇ !!* *_★ 𝙵𝙴𝙴 𝙰𝙳𝙼𝙸𝙼_* *→ 𝟷 - 𝟿 : 𝟷ᴋ* *→ 𝟷𝟶 - 𝟷𝟿 : 𝟸ᴋ* *→ 𝟸𝟶 - 𝟸𝟿 : 𝟹ᴋ* *→ 𝟹𝟶 - 𝟹𝟿 : 𝟺ᴋ* *→ 𝟺𝟶 - 𝟺𝟿 : 𝟻ᴋ* *→ 𝟻𝟶 - 𝟻𝟿 : 𝟼ᴋ* *→ 𝟼𝟶 - 𝟼𝟿 : 𝟽ᴋ* *★ ᴛʀx 𝟷𝟻+ ᴜsᴀʜᴀᴋᴀɴ ᴘᴀᴋᴀɪ ᴀᴅᴍɪɴ ᴜᴛᴀᴍᴀ !!!!* *★ ᴛʀx ʙᴀᴛᴀʟ ғᴇᴇ ᴛᴇᴛᴀᴘ ᴋᴇᴘᴏᴛᴏɴɢ* *★ 𝙽𝙾𝚃𝙴 : 𝙹𝙸𝙺𝙰 𝙾𝚆𝙽 𝙽𝙶𝙴𝚁𝙸𝙿 ? 𝚃𝚄𝙶𝙰𝚂 𝙰𝙳𝙼𝙸𝙽 𝚄𝚃𝙰𝙼𝙰 𝙷𝙰𝙽𝚈𝙰 𝙼𝙴𝙽𝙶𝙰𝙼𝙰𝙽𝙺𝙰𝙽 𝙸𝙳𝙴𝙽𝚃𝙸𝚃𝙰𝚂 !!* *𝙰𝙳𝙼𝙸𝙽 𝚄𝚃𝙰𝙼𝙰 𝚃𝙸𝙳𝙰𝙺 𝙼𝙴𝙽𝙶𝙶𝙰𝙽𝚃𝙸 𝙺𝙴𝚁𝚄𝙶𝙸𝙰𝙽* ✮•━━━━━━━━━━━•-♤•━━━━━━━━━━━━•✮ *★ 𝗥𝗨𝗟𝗘𝗦 𝗚𝗕 𝗟𝗔𝗡𝗚𝗚𝗔𝗥 ? 𝗞𝗜𝗖𝗞 !!!* × ɴᴏ sʜᴀʀᴇ ғᴛ × ɴᴏ sʜᴀʀᴇ ʟɪɴᴋ × ɴᴏ sᴘᴀᴍ sᴛɪᴄᴋᴇʀ × ɴᴏ sʜᴀʀᴇ ᴜɴᴄʜᴇᴄᴋ × ɴᴏ sʜᴀʀᴇ ʙᴇʀʙᴀᴜ 𝟷𝟾+ × ɴᴏ sʜᴀʀᴇ sᴇᴛ ᴀɴᴅʀᴏ / ɪᴘ / ɢs / ʀᴇɢᴇ ᴅʟʟ × sʜᴀʀᴇ ᴊᴀsᴊᴏᴋ 𝟷x ʟɪʜᴀᴛ ──────•+•────── *𝗕𝗘𝗥𝗛𝗔𝗧𝗜-𝗛𝗔𝗧𝗜 𝗧𝗘𝗥𝗛𝗔𝗗𝗔𝗣 𝗖𝗟𝗢𝗡𝗘* ──────•-•────── *#𝗕𝗘 𝗦𝗠𝗔𝗥𝗧 𝗔 𝗕𝗨𝗬𝗘𝗥*

400+ membersILO

NOMALICE E-STORE🛒

✨🔥 *𝔑Ø𝔐𝔞𝔩𝔦𝔠𝔢* *Sales* 🔥✨ 💯 𝐘𝐨𝐮𝐫 𝐍𝐨.𝟏 𝐋𝐞𝐠𝐢𝐭 & 𝐓𝐫𝐮𝐬𝐭𝐞𝐝 𝐅𝐅 𝐕𝐞𝐧𝐝𝐨𝐫 🚀 𝐅𝐚𝐬𝐭 𝐃𝐞𝐚𝐥𝐬 | 𝐅𝐚𝐬𝐭 𝐑𝐞𝐬𝐩𝐨𝐧𝐬𝐞 | 𝐅𝐚𝐬𝐭 𝐃𝐞𝐥𝐢𝐯𝐞𝐫𝐲 🛒 𝐁𝐮𝐲 & 𝐒𝐞𝐥𝐥 𝐅𝐫𝐞𝐞 𝐅𝐢𝐫𝐞 𝐀𝐜𝐜𝐨𝐮𝐧𝐭𝐬 𝐰𝐢𝐭𝐡 𝐂𝐨𝐧𝐟𝐢𝐝𝐞𝐧𝐜𝐞 💎 𝐈𝐧𝐬𝐭𝐚𝐧𝐭 𝐔𝐈𝐃 𝐓𝐨𝐩-𝐔𝐩 & 𝐃𝐢𝐚𝐦𝐨𝐧𝐝𝐬 🔥 𝐁𝐨𝐨𝐬𝐭 𝐘𝐨𝐮𝐫 𝐅𝐅 𝐋𝐢𝐤𝐞𝐬 ✨ Why choose us? ✅ 100% Legit & Trusted MM ✅ Best Deals & Affordable Prices ✅ Smooth, Secure & Hassle-Free Transactions 🤝 𝐃𝐨𝐧’𝐭 𝐠𝐚𝐦𝐛𝐥𝐞 𝐰𝐢𝐭𝐡 𝐬𝐜𝐚𝐦𝐬 — 𝐝𝐞𝐚𝐥 𝐰𝐢𝐭𝐡 𝐭𝐡𝐞 𝐛𝐞𝐬𝐭 💯 🔥 Join the winning side today — *𝔑Ø𝔐𝔞𝔩𝔦𝔠𝔢* *Sales* 𝐠𝐨𝐭 𝐲𝐨𝐮 𝐜𝐨𝐯𝐞𝐫𝐞𝐝! 🔥

300+ membersArabic

FCB AND NOMA MORE UPDATES 🇦🇹🇳🇮⚽⚽🏆🏆

*FCB AND NOMA*༆𝐆𝐑𝐎𝐔𝐏🥰 🌹🌹🌹🌹🌹🌹 *MWALANDILIDWA* *NOSE* *MASUKANI*🔥🔥 ⚠️ *MALAMULO*👇👇 ➡ Ma link a ma group ena ndi remove ❌❌❌ ➡kuponya ma video ampir ✅✅ ➡kunyozan za remove ❌❌❌ ➡Osateng nao mbali pa zochitika za gululi kwa 1 week ndi remove❌❌❌ ➡Ukalowa kumene ponya pic✅ ➡ukalowa gawa link ya group yathu ku ma group ena kapen kwazizanu ngat njila imoz yopitisila la pasogolo group yathuino✅✅✅ ➡ Sunday ndi pic day🔥🔥🔥🔥 👉 Ma video kapena zithuzi zolaula muno ayi ukakamira removal.

200+ membersActive this monthEnglish

Related searches

Sports WhatsApp communitiesAI WhatsApp communitiesBrowse all communities