MALAMULO ATHU ALI MOTERE PA GROUP PANO🔥🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🥳🥳🥳🥳🥳🥳🫠🫠🥳 (1)Sitilora kutumiza ma links ena Muno ukapezeka remove 😡😡 (2)Muno kutumiza nkhani za spots 90% macheza 10% (3)Ndi udindo WA aliyense kutumiza sports osadikira adimin okha okha komanso wa (0 )comment azapangidwa remove (4)Muno ma vn, ma porno,zandale ,zachipembedzo ,ma stickers,timaletsa only sports bas (5)Za ku inbox zithere komko zisafike pa group pano yemwe azapezeke remove (6)
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*MALAMULO ATHU MUNO MU BULLETS MANOMA SILVER 🥈 ZAMASEWERO* ⚽⚽⚽ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena ndi ma sticks ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* mphavu nyerere 🐜🐜🐜🐜🇭🇳🇭🇳🇭🇳🇭🇳 mphavu bullets 🇦🇹🇦🇹🇦🇹🇦🇹 mphave silver 🇦🇷🇦🇷🇦🇷🇦🇷 *umodzi pa machedza* 🤸♂🤸♂🤸♂🤸♂🤸♂
🏆🥈🇦🇹🇪🇺🇧🇼🇮🇴🇵🇫🇬🇱🏆🥇 *MALAMAULO ATHU ALI MOTELE.👇🏻* 🇦🇹 *BULLETS* 🇪🇺 *MANOMA* 🇦🇷 *SILV* 🇬🇷 *BLUE E.* *(( ADMIN WANKULU 👉🏼* *CHANCY HYC* *CHIMA ))* 👨💻🥈 🇦🇹 *MADIMIN ENA ALI MOTELE _MARTIN_ GIFT & NELSON* 👨🎨 ⚽ *Sports* Aliyense Atha Kutumiza always 📻📻🇲🇼 🇪🇺 ```Sapota Ukalowa Tumizani Picture Yako ndi Team Yako. 🇦🇷Kunyozana Kapena Kutukwana Muno Ayi❌ 🇦🇿Tiyeni Tisapote Ma Team athu Monga ndife Amòdzi 🇬🇷Aliyese Azichedza Ndi Nzake Kupewa 👉🏻Remove 🇦🇹Tikakupeza kuti Sukucheza 2 Weeks Yonse👉🏻 Remove 🇪🇺Za ku inbox Zithele Komweko Masapota 🇦🇿Nthawi Ya Game aliyeee Atha kutumiza Zotsatira 🇦🇷Vn Muno ayi ❌ 🇬🇷Nyimbo Tumizani any Song. Bola osapyola muyeso English muno ayi mlibe azungu 🇲🇼 ❌ Zandale ayi ukapedzeka ndi remove 🇲🇭❌ Ngat ukubwela ndichisokonedzo remove ❌🇲🇼 NGAT PALI VUTO PENA OR SIMUNAVETSE FUSANI MA ADIMIN ALIPO KUT ATITHANDIZE 🛡️🇲🇼 🇸🇽NO MA VIDEO OLAULA MUNO MA PORNO AI ❌ ® Martin@ ma adimin wotse tigwile ntchito molimbika pamozi ndima members athu 🇲🇼 Sports parliament, ZBS sports, times sports bembeke sports,⚽🏐🛡️🇲🇼🔥🔥ndingot mwakoma notse buy buy 🙏
To join our newsgroup go to the below link and be fully informed of what is really happening in Israel and the World. [link hidden — subscribe to view]?mode=ac_t
NBB🇦🇹🇦🇹NOMA🇪🇺🇪🇺SILVER STRIKERS🇧🇼🇧🇼 Takulandilan ku group la masapota ampira okonda ma team awo mwamtendere. Muno timalimbikisa kukondana wina ndi mzake osat mikangano koma macheza okhuza mpira bas. Ochilimika kuponya nkhan pazikhakala mwayi wa mphoto ya ma bundle a internet *Malamulo agroup lino* Zolesedwa 1.osaponya link la group Lina ❌❌❌❌ukatero remove 2.osaponya chilichonse choonesa kulaula❌❌❌❌ukatero remove 3.osachula maina oyambisa mikangano muno monga:kapado/nkhumba fc,chingambwe fc,nyau fc❌❌❌❌ ukapezeka remove. 4.osaponya ma sticker,voice note,kutukwana❌❌❌❌Ukapezeka remove 5.siku la mpira(match day)ndi siku longoponya ma updade osasakaniza nkhan kupereka mpata kwa mamembala kusatira mpira. 6.kupereka update yabodza❌❌❌❌ Ukapezeka remove 7.kusakhala active kwa 2weeks❌❌❌❌remove 8.Ili ndi group la za mpira only osatumiza zosemphana ndi mpira monga za ndale,nkhan osat zampira❌❌❌❌ukapezeka remove 9.ukalowa pa chat kukakhala game tiziyesesa kusatila mamessage omwe atizidwa kale kut tione mmene ma results mmene akuyendera kupewa mafunso ot game ikuyenda bwanji,wagolesa ndan,zikutha bwanji,izi zimapwetekesa omwe amuluza. 11.oyambisa chisokonezo muno❌❌❌❌remove *Kutumiza nkhan ndi kwa aliyense osadikilira ma admin okha* Ngat mwawona vuto pa malamulowa pezanani ndi admin ndipo tulani nkhawa zanu. Masiku ena tizikhala ndi mway ocheza ndi alendo koma a mpira okhaokha. *Maule,manoma ndi ma bankers 🚩🚩🚩🇦🇹🇦🇹🇬🇷🇬🇷🇬🇷🇪🇺🇪🇺🇪🇺🇧🇼🇧🇼🇧🇼🇧🇼pamodz imapanga flames🇲🇼* Zikomo khalan omasuka *By adminstration*
*_Yᴏᴜʀ ʟᴏsᴇ ᴏᴜʀ ᴘʀɪᴏʀɪᴛʏ😀👍_* *_RULES FOR AGAINST SUPPORTERS UNION_* 1️⃣English only please and We are not English teachers learn to accomodate people of different languages as they try to discuss in English 2️⃣No promotion of links (group/spam). 3️⃣Only footballers pictures are allowed 4️⃣Make sure u are part of the group conversations. 5️⃣Feel free to troll clubs. 6️⃣Feel free to post football updates. 7️⃣No Political Talks❌ 8️⃣Don't abuse any group member. 9️⃣ Posts must be in tandem with football 1️⃣0️⃣Repeat and chronic offenders will be banned permanently 1️⃣2️⃣Respect all members and admins regardless of age, gender, race, nationality and tribe 1️⃣3️⃣No nude pictures and porn videos allowed. posting porn stuff in the group will lead to immediate removal 1️⃣4️⃣Please do not discuss any religious matters or political parties in the group 1️⃣5️⃣Address your fellow members and admins with respect *NOTE:* *WE SET RULES FOR A PURPOSE IF U CANT FOLLOW OUR RULES DONT JOIN US*
*WELCOME TO 🇦🇹BULLETS+SILVER+WANDERERS 🇦🇷AND OTHER SPORTS UPDATES‼️* 🥇 ⚽ ```AWA NDIWO MALAMULO APAMUDZI PANO WERENGANI MODEKHA KUTI MUTSATIRE NDONDOMEKO ZOYENERA KUCHITA MUKALOWA👇👇👇``` *⚠️Ziyankhuro zoloredwa muno ndi CHICHEWA+ENGLISH basi ukapezeka ukutumiza zosamveka Out❌* *●Ma Link a ma group ena❌* *●Ma Stickers❌* *●Ma porn or Nude pic❌* *•Kuponya Update Yabodza❌* *●Ma Voice Note❌* *●Kunyozana muno❌* *●Kusankha munthu omacheza naye muno❌* *Tonse ndife amodzi* *●Khalani omasuka bola osanyula(Kuphwanya Lamulo(* *WELCOME TO 🇦🇹BULLETS+SILVER+WANDERERS 🇦🇷AND OTHER SPORTS UPDATES‼️* 🥇 ⚽ ```AWA NDIWO MALAMULO APAMUDZI PANO WERENGANI MODEKHA KUTI MUTSATIRE NDONDOMEKO ZOYENERA KUCHITA MUKALOWA👇👇👇``` *⚠️Ziyankhuro zoloredwa muno ndi CHICHEWA+ENGLISH basi ukapezeka ukutumiza zosamveka Out❌* *●Ma Link a ma group ena❌* *●Ma Stickers❌* *●Ma porn or Nude pic❌* *•Kuponya Update Yabodza❌* *●Ma Voice Note❌* *●Kunyozana muno❌* *●Kusankha munthu omacheza naye muno❌* *Tonse ndife amodzi* *●Khalani omasuka bola osanyula(Kuphwanya Lamulo(* ⚫ *TIYENI TIZIPANGANA SURPORT MUNTHU AKAPONYA UPDATE KUTI GROUP LIZIPITA PATSOGOLO OSATI KUSANKHANA AYI....🙏🙏🙏"* *MUKAPEZA VUTO MUNO(GROUP) MUPEZENI ADMIN ALIYENSE AZAKUTHANDIZANI KUKONZA VUTOLO🙏🙏🙏* *🇦🇹BULLETS+WANDERERS+SILVER 🇦🇷AND ALL OTHER SPORTS UPDATES ADMINSTRATION DESK* ⚫ *TIYENI TIZIPANGANA SURPORT MUNTHU AKAPONYA UPDATE KUTI GROUP LIZIPITA PATSOGOLO OSATI KUSANKHANA AYI....🙏🙏🙏"* *MUKAPEZA VUTO MUNO(GROUP) MUPEZENI ADMIN ALIYENSE AZAKUTHANDIZANI KUKONZA VUTOLO🙏🙏🙏* *🇦🇹BULLETS+WANDERERS+SILVER 🇦🇷AND ALL OTHER SPORTS UPDATES ADMINSTRATION DESK* 🍿🥎⚾🥍🏈🏐⚽⚽⚽🏸