*yang real ada marcelreyzz !!* this is gl not cc/marga optes nunggu admin opn optes isian/ga tergantung admin! [contact hidden] all wajib win! rules: wajib out dari gl lain sblm tes high mekanik ss prof level akun 50+ only mid no bokong/zona skill r https sc diss ›link gb opmem‹ [link hidden — subscribe to view]
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*MALAMULO ATHU MUNO MU BULLETS MANOMA SILVER 🥈 ZAMASEWERO* ⚽⚽⚽ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena ndi ma sticks ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* mphavu nyerere 🐜🐜🐜🐜🇭🇳🇭🇳🇭🇳🇭🇳 mphavu bullets 🇦🇹🇦🇹🇦🇹🇦🇹 mphave silver 🇦🇷🇦🇷🇦🇷🇦🇷 *umodzi pa machedza* 🤸♂🤸♂🤸♂🤸♂🤸♂
MALAMULO ATHU ALI MOTERE PA GROUP PANO🔥🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🥳🥳🥳🥳🥳🥳🫠🫠🥳 (1)Sitilora kutumiza ma links ena Muno ukapezeka remove 😡😡 (2)Muno kutumiza nkhani za spots 90% macheza 10% (3)Ndi udindo WA aliyense kutumiza sports osadikira adimin okha okha komanso wa (0 )comment azapangidwa remove (4)Muno ma vn, ma porno,zandale ,zachipembedzo ,ma stickers,timaletsa only sports bas (5)Za ku inbox zithere komko zisafike pa group pano yemwe azapezeke remove (6)
To join our newsgroup go to the below link and be fully informed of what is really happening in Israel and the World. [link hidden — subscribe to view]?mode=ac_t
*OPMEM THREEHARD ALL CABANG* *FOUNDER GL : @1yannn @manz* *OWN BOY : @piki @valzy @rey* *OWN LDS : @cimiy* *- BUY SLOT MEM/PETINGGI/PENGURUS/OWN/TANGAN KANAN* *- BIKIN CABANG THREEHARD* [link hidden — subscribe to view] *[1YANNN]* [link hidden — subscribe to view] *[MANZ]* [link hidden — subscribe to view] *[PIKI]* [link hidden — subscribe to view] *[VALZY]* [link hidden — subscribe to view] *[CIMIY]* *SISTEM OPTES :* ISIAN/FREE TERGANTUNG ADMIN 11 5+ 22 10+ jago? lolos *SYARAT OPREK :* - foll tt 500+/on tiktok - bawa gp *RULES OPTES :* - 11/22 no zona - opt dlm gl dis no drama - opt wajib ss 00 - nvmtps - admin score 6 ga lolos - minim win 7-5 lolos - high mekanik - minim level 50+ / tergantung admin mau nerima atau ga *GOOD LUCK DITUNGGU DI ALLBASE* *GB OPMEM THREEHARD ALL CAB 1 :* [link hidden — subscribe to view] *GB OPMEM THREEHARD ALL CAB 2 :* [link hidden — subscribe to view] *GB OPMEM THREEHARD ALL CAB 3 :* [link hidden — subscribe to view] *GB OPMEM THREEHARD LDS :* [link hidden — subscribe to view]
NBB🇦🇹🇦🇹NOMA🇪🇺🇪🇺SILVER STRIKERS🇧🇼🇧🇼 Takulandilan ku group la masapota ampira okonda ma team awo mwamtendere. Muno timalimbikisa kukondana wina ndi mzake osat mikangano koma macheza okhuza mpira bas. Ochilimika kuponya nkhan pazikhakala mwayi wa mphoto ya ma bundle a internet *Malamulo agroup lino* Zolesedwa 1.osaponya link la group Lina ❌❌❌❌ukatero remove 2.osaponya chilichonse choonesa kulaula❌❌❌❌ukatero remove 3.osachula maina oyambisa mikangano muno monga:kapado/nkhumba fc,chingambwe fc,nyau fc❌❌❌❌ ukapezeka remove. 4.osaponya ma sticker,voice note,kutukwana❌❌❌❌Ukapezeka remove 5.siku la mpira(match day)ndi siku longoponya ma updade osasakaniza nkhan kupereka mpata kwa mamembala kusatira mpira. 6.kupereka update yabodza❌❌❌❌ Ukapezeka remove 7.kusakhala active kwa 2weeks❌❌❌❌remove 8.Ili ndi group la za mpira only osatumiza zosemphana ndi mpira monga za ndale,nkhan osat zampira❌❌❌❌ukapezeka remove 9.ukalowa pa chat kukakhala game tiziyesesa kusatila mamessage omwe atizidwa kale kut tione mmene ma results mmene akuyendera kupewa mafunso ot game ikuyenda bwanji,wagolesa ndan,zikutha bwanji,izi zimapwetekesa omwe amuluza. 11.oyambisa chisokonezo muno❌❌❌❌remove *Kutumiza nkhan ndi kwa aliyense osadikilira ma admin okha* Ngat mwawona vuto pa malamulowa pezanani ndi admin ndipo tulani nkhawa zanu. Masiku ena tizikhala ndi mway ocheza ndi alendo koma a mpira okhaokha. *Maule,manoma ndi ma bankers 🚩🚩🚩🇦🇹🇦🇹🇬🇷🇬🇷🇬🇷🇪🇺🇪🇺🇪🇺🇧🇼🇧🇼🇧🇼🇧🇼pamodz imapanga flames🇲🇼* Zikomo khalan omasuka *By adminstration*
╭────────────╮ 𝐕𝐢𝐧 𝐞𝐧𝐭𝐞𝐫𝐭𝐚𝐢𝐧𝐦𝐞𝐧𝐭 ╰────────────╯ ```#JANGAN SPAM.``` ```#DON'T MENTION GRUP OR KICK‼️``` *𝐎𝐅𝐂 𝐘𝐎𝐔𝐓𝐔𝐁𝐄 𝐕𝐈𝐍 𝐄𝐍𝐓𝐄𝐑𝐓𝐀𝐈𝐍𝐌𝐄𝐍𝐓* https://www.youtube.com/@vinentofc *new account* https://www.youtube.com/@vinenter12 *𝐎𝐅𝐂 𝐈𝐍𝐒𝐓𝐀𝐆𝐑𝐀𝐌 𝐕𝐈𝐍 𝐄𝐍𝐓𝐄𝐑𝐓𝐀𝐈𝐍𝐌𝐄𝐍𝐓* https://instagram.com/vinentertainment_ofc?igshid=YmMyMTA2M2Y= *new account* https://instagram.com/vin_entertainment2022?igshid=MGNiNDI5ZTU= *𝐎𝐅𝐂 𝐓𝐈𝐊𝐓𝐎𝐊 𝐕𝐈𝐍 𝐄𝐍𝐓𝐄𝐑𝐓𝐀𝐈𝐍𝐌𝐄𝐍𝐓* tiktok.com/@ofcvinent *𝐋𝐈𝐍𝐊 𝐋𝐏𝐌* [link hidden — subscribe to view]