CommunitiesSilver Glitz

Silver Glitz

100+ membersDAN

About this community

Original Aqeeq , Turquoise, Dur e Najaf & more exclusive. 925 Sterling Silver | Rhodium coated ( tanish free)

DAN
Unlock / View Community

Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.

Related communities

BULLETS ♉ MANOMA 💙 SILVER 🥈 ZAMASEWERO

*MALAMULO ATHU MUNO MU BULLETS MANOMA SILVER 🥈 ZAMASEWERO* ⚽⚽⚽ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena ndi ma sticks ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* mphavu nyerere 🐜🐜🐜🐜🇭🇳🇭🇳🇭🇳🇭🇳 mphavu bullets 🇦🇹🇦🇹🇦🇹🇦🇹 mphave silver 🇦🇷🇦🇷🇦🇷🇦🇷 *umodzi pa machedza* 🤸‍♂🤸‍♂🤸‍♂🤸‍♂🤸‍♂

900+ membersBUG

🔥⚽🇲🇼 NBB VS NOMA $ SILVER SUPPORTERS GROUP ( A)🔥⚽🔥🇲🇼🔥🇿🇦

MALAMULO ATHU ALI MOTERE PA GROUP PANO🔥🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🥳🥳🥳🥳🥳🥳🫠🫠🥳 (1)Sitilora kutumiza ma links ena Muno ukapezeka remove 😡😡 (2)Muno kutumiza nkhani za spots 90% macheza 10% (3)Ndi udindo WA aliyense kutumiza sports osadikira adimin okha okha komanso wa (0 )comment azapangidwa remove (4)Muno ma vn, ma porno,zandale ,zachipembedzo ,ma stickers,timaletsa only sports bas (5)Za ku inbox zithere komko zisafike pa group pano yemwe azapezeke remove (6)

900+ membersSWE

Alan Silver IV Newsgroup

To join our newsgroup go to the below link and be fully informed of what is really happening in Israel and the World. [link hidden — subscribe to view]?mode=ac_t

800+ membersNNO

NBB🚩🚩🚩🇦🇹🇦🇹 NOMA🇪🇺🇪🇺🇬🇷🇬🇷 SILVER🇧🇼🇧🇼🇧🇼

NBB🇦🇹🇦🇹NOMA🇪🇺🇪🇺SILVER STRIKERS🇧🇼🇧🇼 Takulandilan ku group la masapota ampira okonda ma team awo mwamtendere. Muno timalimbikisa kukondana wina ndi mzake osat mikangano koma macheza okhuza mpira bas. Ochilimika kuponya nkhan pazikhakala mwayi wa mphoto ya ma bundle a internet *Malamulo agroup lino* Zolesedwa 1.osaponya link la group Lina ❌❌❌❌ukatero remove 2.osaponya chilichonse choonesa kulaula❌❌❌❌ukatero remove 3.osachula maina oyambisa mikangano muno monga:kapado/nkhumba fc,chingambwe fc,nyau fc❌❌❌❌ ukapezeka remove. 4.osaponya ma sticker,voice note,kutukwana❌❌❌❌Ukapezeka remove 5.siku la mpira(match day)ndi siku longoponya ma updade osasakaniza nkhan kupereka mpata kwa mamembala kusatira mpira. 6.kupereka update yabodza❌❌❌❌ Ukapezeka remove 7.kusakhala active kwa 2weeks❌❌❌❌remove 8.Ili ndi group la za mpira only osatumiza zosemphana ndi mpira monga za ndale,nkhan osat zampira❌❌❌❌ukapezeka remove 9.ukalowa pa chat kukakhala game tiziyesesa kusatila mamessage omwe atizidwa kale kut tione mmene ma results mmene akuyendera kupewa mafunso ot game ikuyenda bwanji,wagolesa ndan,zikutha bwanji,izi zimapwetekesa omwe amuluza. 11.oyambisa chisokonezo muno❌❌❌❌remove *Kutumiza nkhan ndi kwa aliyense osadikilira ma admin okha* Ngat mwawona vuto pa malamulowa pezanani ndi admin ndipo tulani nkhawa zanu. Masiku ena tizikhala ndi mway ocheza ndi alendo koma a mpira okhaokha. *Maule,manoma ndi ma bankers 🚩🚩🚩🇦🇹🇦🇹🇬🇷🇬🇷🇬🇷🇪🇺🇪🇺🇪🇺🇧🇼🇧🇼🇧🇼🇧🇼pamodz imapanga flames🇲🇼* Zikomo khalan omasuka *By adminstration*

600+ membersZUL

Glitz and glam kaftans ✨️

Glits & Glam ,where style meets the streets! ✨ Your mobile boutique for trendy, affordable fashion delivered with sparkle and convenience. We bring the glam to your doorstep because every day deserves a little shimmer 😊

600+ membersEnglish

🔥🇦🇹BULLETS+🔥🇦🇷SILVER🔥+🇸🇻WANDERERS🔥 & CIVIL 🔥ALL SPORTS UPDATES⚽🏐🏀🔥🔥

*WELCOME TO 🇦🇹BULLETS+SILVER+WANDERERS 🇦🇷AND OTHER SPORTS UPDATES‼️* 🥇 ⚽ ```AWA NDIWO MALAMULO APAMUDZI PANO WERENGANI MODEKHA KUTI MUTSATIRE NDONDOMEKO ZOYENERA KUCHITA MUKALOWA👇👇👇``` *⚠️Ziyankhuro zoloredwa muno ndi CHICHEWA+ENGLISH basi ukapezeka ukutumiza zosamveka Out❌* *●Ma Link a ma group ena❌* *●Ma Stickers❌* *●Ma porn or Nude pic❌* *•Kuponya Update Yabodza❌* *●Ma Voice Note❌* *●Kunyozana muno❌* *●Kusankha munthu omacheza naye muno❌* *Tonse ndife amodzi* *●Khalani omasuka bola osanyula(Kuphwanya Lamulo(* *WELCOME TO 🇦🇹BULLETS+SILVER+WANDERERS 🇦🇷AND OTHER SPORTS UPDATES‼️* 🥇 ⚽ ```AWA NDIWO MALAMULO APAMUDZI PANO WERENGANI MODEKHA KUTI MUTSATIRE NDONDOMEKO ZOYENERA KUCHITA MUKALOWA👇👇👇``` *⚠️Ziyankhuro zoloredwa muno ndi CHICHEWA+ENGLISH basi ukapezeka ukutumiza zosamveka Out❌* *●Ma Link a ma group ena❌* *●Ma Stickers❌* *●Ma porn or Nude pic❌* *•Kuponya Update Yabodza❌* *●Ma Voice Note❌* *●Kunyozana muno❌* *●Kusankha munthu omacheza naye muno❌* *Tonse ndife amodzi* *●Khalani omasuka bola osanyula(Kuphwanya Lamulo(* ⚫ *TIYENI TIZIPANGANA SURPORT MUNTHU AKAPONYA UPDATE KUTI GROUP LIZIPITA PATSOGOLO OSATI KUSANKHANA AYI....🙏🙏🙏"* *MUKAPEZA VUTO MUNO(GROUP) MUPEZENI ADMIN ALIYENSE AZAKUTHANDIZANI KUKONZA VUTOLO🙏🙏🙏* *🇦🇹BULLETS+WANDERERS+SILVER 🇦🇷AND ALL OTHER SPORTS UPDATES ADMINSTRATION DESK* ⚫ *TIYENI TIZIPANGANA SURPORT MUNTHU AKAPONYA UPDATE KUTI GROUP LIZIPITA PATSOGOLO OSATI KUSANKHANA AYI....🙏🙏🙏"* *MUKAPEZA VUTO MUNO(GROUP) MUPEZENI ADMIN ALIYENSE AZAKUTHANDIZANI KUKONZA VUTOLO🙏🙏🙏* *🇦🇹BULLETS+WANDERERS+SILVER 🇦🇷AND ALL OTHER SPORTS UPDATES ADMINSTRATION DESK* 🍿🥎⚾🥍🏈🏐⚽⚽⚽🏸

500+ membersActive this monthDAN