Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ TAKULANDIRANI PANO PA F C B NYASA BG BULLETS GROUP ๐ฟ NTHAWI IKAKWANA ๐๐๐๐ฅ 10:30 PM GROUP LINO LIDZITSEKEDWA POFUNA KUTETEZA GROUP LINO KWA ANTHU OMWE AMAKONDA KUTUMIZA ZITHU ZOSAKHARA BWINO ANTHU AKAGONA M'MA GROUP NDIPO LIDZITSEKULIDWA๐๐๐ฅ 5:30AM NDIPO MARAMURO ALI MOTERE ๐ ๐ ๐ ๐ ๐ SUNDAY LILILONSE MUZIYENDA CHIKOLOPA MUNO KUSABURA AMENE SAKUTENGA NAWO GAWO MUNO ๐ซต ๐ซต ๐ซต ๐ซต ๐ซต ๐ซต ๐ซต ๐ซต ๐ซต DZIWANI KUTI UKAPEZEKA PANO UKUYENERA KUMATENGA NAWO GAWO PA NKHANI ZAMASEWERO KOMASO MACHEZA FOLLOW ๐๐๐๐๐๐ฅ RAMULO (1). OSATUMIZA MA BUSINESS KAPENA ZA USING'ANGA MUNO โ RAMULO (2). OSATUMIZA MA LINK AMA GROUP ENA MUNO โ RAMULO (3). OSATUKWANA MUNO โKAPENA KUNYOZERANA ZIPEMBEDZO โ RAMULO (4). OSATUMIZA NKHANI ZOPANDA UMBONI MUNO โ RAMULO (5). OSARANKHURA VN MUNO NGATI USANAPEPHE CHILOLEZO KWA ADMIN โ SUNDAY LILILONSE MUZIYENDA CHIKOLOPA MUNO KUSABURA AMENE SAKUTENGA NAWO GAWO ๐ซต ๐ซต ๐ซต ๐ซต ๐ซต RAMULO (6). OSAIMBA GROUP CALL MUNO โ RAMULO (7). NDI UFULU WANU KUTUMIZA NKHANI ZAMASEWERO โ KUCHOKERA PA WAIRES ZOSIYANA SIYANA ANGAKHARESO MA CHANNEL OSIYANA SIYANAโ RAMULO (8). OSATUMIZA MA VIDEO ORAULA KOMASO MA PHOTO MUNO โ TENGANI GAWO PA NKHANI ZAMASEWERO NGAT ULI SAPOTA WENI WENI WA BULLETS ๐ฎ๐ฉ TIYENI TITSATILE MARAMURO POFUNA KULIMBIKITSA UMODZI, CHIKONDI, NDI CHIKOKA CHA GROUP LINO TIMAKUNYADIRANI MAPARE STNA ANZATHU ๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฎ๐ฉ๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ ๐๏ธ ๐๏ธ ๐๏ธ ๐๏ธ ๐๏ธ ๐๏ธ ๐๏ธ ๐๏ธ โฝ โฝ โฝ โฝ โฝ โฝ โฝ โฝ ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*MALAMULO ATHU MUNO MU BULLETS MANOMA SILVER ๐ฅ ZAMASEWERO* โฝโฝโฝ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena ndi ma sticks ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* mphavu nyerere ๐๐๐๐๐ญ๐ณ๐ญ๐ณ๐ญ๐ณ๐ญ๐ณ mphavu bullets ๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น mphave silver ๐ฆ๐ท๐ฆ๐ท๐ฆ๐ท๐ฆ๐ท *umodzi pa machedza* ๐คธโโ๐คธโโ๐คธโโ๐คธโโ๐คธโโ
1๏ธโฃOsasitha chithuzi kapena mutu wa gulu 2โฃMa videos olaula muno ayi or pic. 3๏ธโฃOsatumiza link ya group lina muno ayinso 4๏ธโฃNo voice messages /stickers ๐ฏ. 5๏ธโฃMuno simosewela koma kugawana Sports ndi Tinkhani patali patali 6๏ธโฃkumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa. 7๏ธโฃUlemu kwa aliyese. 8๏ธโฃNkhan zaku inbox zithere Komweko. 9๏ธโฃNgati member wa group waona povuta pena pake pita kwa admin aliyese muuze kuti akuthandize ๐ Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi. 11. Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja ๐ *By Admin*